Chichewa
-
Mapemphero a mvula aliko lero
Pamene ng’amba yadzetsa chikaiko choti Amalawi akhoza kukolola zochepa chaka chino, mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika lero akhala nawo…
Read More » -
Njovu ipha mlenje
Tsoka sasimba. Akanadziwa mlenje sakadapita kunkhalango ya Liwonde kukasaka nyama mozemba masiku apitawo. Patrick Maya, wa zaka 52, ndipo amachokera…
Read More » -
Si zonyengerera mu 2016—Mkulu wa polisi
Anthu ali kalikiriki kukonza mapulani a chaka chatsopano cha 2016 koma ngati mapulani ake akukhudza umbanda ndi ziphuphu, dziko lake…
Read More » -
Adakumana bwanji m’chakacho?
Ankadzapepesa maliro a mkazi wanga’ Ukwati ndi chinthu chabwino, ndipo Mulungu amasangalala nacho. Chaka cha 2015 Mulungu adadalitsa ena ndi…
Read More » -
A Malawi adalimba nazo chaka chatha
Ululu, kulavulagaga ndi kupala moto kudalipo mchaka chomwe changothachi monga momwe akadaulo mnthambi zosiyanasiyana akunenera kuti padalibe popumira koma kubanika…
Read More » -
Mudalinji m’chakachi?
Ma alubino aona zakuda Mpotopola ku Joni, Amalawi 3 200 athothedwa Anthu 106 afa ndi madzi osefukira Tili m’chaka…
Read More » -
Tidacheza nawo bwanji?
M’chaka cha 2015 tamva zikhulupiriro, miyambo komanso mbiri zosiyanasiyana za maderanso osiyana. Lero BOBBY KABANGO akutibweretsera macheza ochepa amene nkhani…
Read More » -
Kupewa nsabwe za m’fodya ndi pano
Nsabwe za mufodya ndi gwero limodzi lomwe limachititsa kuti fodya avute malonda kumsika ndipo vutoli likagwera mlimi, chaka chimenecho amalirira…
Read More » -
Mmera watuluka koma samalani, atero katswiri
Mmera watuluka ndipo momwe zikuonekera alimi ambiri akhoza kuchita mphumi chaka chino zinthu zikapanda kusintha, makamaka pakagwedwe ka mvula. Koma…
Read More » -
Abambo odzikhweza akuchuluka
Kafukufuku wa apolisi m’dziko muno waonetsa kuti abambo 90 ndiwo amadzipha pa anthu 100 alionse amene amatenga miyoyo yawo…
Read More » -
Kalonga: Waluso lothetsa makhalu
Kunja kuno oimba ndiye mbwee koma luso lawo limakhala losiyanasiyana. Ena ali ndi mawu anthetemya, ena amaimba zipangiso monga zing’wenyeng’wenye,…
Read More » -
ANATCHEZERA
Nditenge uti? Anatchereza, Munthune ndili ndi zibwenzi ziwiri. Zonsezi zidayamba chaka chimodzi panopa zatha zaka zitatu ndipo onsewa ndimawakonda chimodzimodzi…
Read More » -
Ankadziwana ndi mayi anga’
Kale makolo amachita kusankhira ana awo munthu wokwatirana naye, koma pano zinthu zidasintha ngakhale kuti makolowo akhoza kungokhala muni…
Read More » -
Apumphuntha ana ndi nsimbi
Ana atatu a banja limodzi abwerera lokumbakumba mayi wawo Eveter Kulemera, wa zaka 24, akuti atawalumira mano kuwapumphuntha ndi…
Read More » -
Adona Hilida akadangobwera
Ngakhale pa Wenela padali zovuta, malo aja timakonda padali kuphulika nyimbo. Ine nilibe pulobulemu Nilibe pulobulemu…. Chifukwatu timayembekezera kuti wotisiyayo…
Read More » -
Khama lipindula paulimi—Phungu
Nthawi zambiri chomwe chimasowa paulimi ndimasomphenya. Alimi ambiri amangolingalira zoti ndikakolola chaka chino ndidzalimanso chaka cha mawa mmalo moti azilingalira…
Read More » -
Chipongwe m’maofesi mwinamu
Pali maofesi angapo, maka a boma, omwe amachuluka chipongwe kaya titi mwano polankhula ndi anthu ofuna chithandizo. Ofesi ngati za…
Read More » -
Chidyaabusa: Nthumbwana yofewetsetsa
Zamkati mwa nyama monga ng’ombe kapena mbuzi zija ena amati nthumbwana ndi ndiwo zofewa zomwe ambiri amakonda kupatsa mafumu kapena…
Read More » -
Ziweto zisasowe mtendere m’khola
yengo ya mvula ino, ziweto monga ng’ombe, mbuzi, nkhosa ndi nkhumba zimasauka kaamba ka matope m’khola, zomwe zimachititsa kuti…
Read More » -
Bungwe lilangiza alimi kubzala mbewu zopirira
Malingana ndi kabweredwe ka mvula ya masiku ano, akatswiri alimbikitsa kuti alimi asamangoganiza za mbewu zamakono koma mbewuzo zizikhala…
Read More »