Chichewa
-
Siyayo Mkandawire atisiya
Thambo lagwa kubanja la a Mkandawire a m’mudzi wa Zebera m’dera la Mfumu Yaikulu M’mbwelwa m’boma la Mzimba komwe…
Read More » -
Mswati adakali mfumu—Boma
Boma, kudzera mwa mneneri wa unduna wa maboma aang’ono ke Muhlabase Mughogho, lati ngakhale pali kukokanakokana pa ufumu wa Gomani…
Read More » -
Maphunziro alowa nthenya
…Okhudzidwa ndi ngozi akuphuphabe Nthawi ili cha m’ma hafu pasiti leveni (11:30 am) ndipo kunja kukutentha koopsa. Ena mwa ophunzira…
Read More » -
‘Fodya n’kunazale’
Pamene alimi a fodya ali yakaliyakali kukonzekera ulimi wa 2015/16, mlangizi wa zaulimi wa fodya m’boma la Rumphi, Charles Jere,…
Read More » -
Zakudya za ziweto zasowa
M’boma la Nsanje, ziweto monga ng’ombe, nkhosa ndi mbuzi zili pamoto chifukwa cha kusowa kwa chakudya. Kwauma, ndipo tchire anthu…
Read More » -
Chotsani ndale mu ulimi wamthirira—Jalavikuba
Inkosi Jalavikuba ya m’boma la Mzimba yapempha boma kuika alimi patsogolo ndi kuchotsa ndale muulimi wamthirira. Mfumuyi idanena izi Loweruka…
Read More » -
Mlaliki wozizwitsa pa Wenela
Tsikulo pa Wenela padali mapemphero. Abale anzanga kwadzatu alaliki. Koma ine sindiiwala ntchito za ulaliki za Shadreck Wame amene…
Read More » -
Wofuna kuba alubino amusinthira mlandu
Mkulu yemwe akuimbidwa mlandu wofuna kuba alubino ndi cholinga chomupha zidamuthina Lachiwiri lapitali kubwalo la milandu la majisitireti ku Mzuzu…
Read More » -
‘Aoloka yorodani’ pamtsinje wa ruo
Sukulu adalekera sitandade 4, kuwerenga n’komuvuta, koma kuwerengera ndalama kwa iye si nkhani. Ngakhale sukulu sadapite nayo patali, ntchito…
Read More » -
Gayighaye Mfune: Wosula oimba
Kuimba ndi luso lomwe ena amabadwa nalo pomwe ena amachita kuphunzira. Maphunziro a zoimbaimba amachuluka zifanifani ndipo zimatengera luso la…
Read More » -
Anatchezera
Sakundikwatira Agogo, Ndithandizeni. Ndili paubwenzi ndi mwamuna yemwe adakwatirapo koma banja lake lidatha ndi mkaziyo ndipo kuli mwana mmodzi. Inenso…
Read More » -
Boma likukhazikitsa misika ya zakudimba
Boma lili mkati momanga malo ogulitsira zokolola zakudimba ngati njira imodzi yochulukitsira phindu lomwe alimi amapeza pogulitsa zokolola zochokera mu…
Read More » -
Alimi avale dzilimbe, kukubwera El Nino
Akatswiri a zanyengo alosera kuti chaka chino pali mantha kuti dziko lino lingakumane ndi nyengo yoipa ya El Nino. Lipoti…
Read More » -
Boma litemera ziweto 10 000
Pofuna kuthana ndi mliri wa matenda a zilonda za m’ mapazi ndi m’mkamwa a ng’ombe omwe agwa m’boma la Chikwawa,…
Read More » -
Malawi sisewera ndi Uganda
Chiyembekezo chidalipo kuti Malawi iswana ndi Uganda kuti ikonzekere masewero a World Cup pa 7 October pamene ikunthane ndi Tanzania.…
Read More » -
Mwambo ‘wopha mudzi’ poika mfumu
Anthu ena amakhulupirira kuti akamwalira amayenera akaikidwe chatsonga kapena kuti chokhala. Izi zimachitika kwambiri pakati pa mafumu Achingoni maka a…
Read More » -
Adutse ndani mu Standard Bank?
Ndime ya kotafainolo mu Standard Bank Cup yafika podetsa nkhawa pamene matimu anayi akuyenera kutsanzikana ndi chikhochi sabata ino. Pamene…
Read More » -
Mavuto a madzi akula mu October ku Lilongwe
Pomwe anthu mumzinda wa Lilongwe akubangula ndi vuto la kuzimazima kwa magetsi, kampani yopereka madzi ya Lilongwe Water Board yachenjeza…
Read More » -
Anjata wopezeka ndi mitengo ya tsanya
Apolisi ku Lilongwe Lachitatu adanjata nzika ya ku China chifukwa chomuganizira kuti adapezeka ndi mitengo ya tsanya yomwe nzikayo imafuna…
Read More » -
‘Chidwi pantchito ya uphunzitsi chizilala’
Bungwe la aphunzitsi m’dziko muno la Teachers Union of Malawi (TUM) lati zomwe lachita boma pokhazikitsa mfundo yoti ofuna kuphunzira…
Read More »