Nkhani
-
Low turnout as voter registrationfor March 17 by‑elections opens
Voter registration for the March 17 by‑elections opened on a muted note with several registration centres recording little or no…
Read More » -
Adagona ndi mwana, kapena ayi?
Zodulitsa mutu wa zizwa. Pomwe bwalo la milandu la majisitileti ku Mchinji lidagamula kuti a Ernest Chimpeni a zaka 37…
Read More » -
Chimanga ‘amachibisa’ chatuluka
Patangotha masiku ochepa boma litayamba kulandira chimanga chomwe lagula m’dziko la Zambia, mavenda nawo atulutsa chimanga chawo chomwe akufuna kukagulitsa…
Read More » -
Kulembetsa ndi lero
Kalembera wa Chisankho Chapadera cha pa 17 March chikubwerachi ayamba lero m’madera a aphungu 4 ndi makhansala 9 m’maboma 12…
Read More » -
Samalani, kunjaku kwabuka cholera
Boma lalandira matamando pa momwe layendetsera dziko m’masiku 100 oyambirira koma malesawa akumana n’chipsinjo cha matenda a cholera omwe abuka…
Read More » -
Zaka zisanu chifukwa choba katundu
Bwalo la First Grade Magistrate ku Lilongwe, Lachinayi lidagamula Mayi Esther James a zaka 38 kuti akakhale ku ndende kwa…
Read More » -
Aika makamera m’ndende
Mabungwe omenyera ufulu wa anthu alandira ndi manja awiri ganizo la nthambi ya za ndende loika makamera m’ndende ngati njira…
Read More » -
Bilu ya CDF yatsamwa
Mabungwe omwe si aboma ayamikira a Pulezidenti a Peter Mutharika pokana kusainira bilu yofuna kuti aphungu aziyendetsa thumba la chitukuko…
Read More » -
Sangalalani mosamala
Pomwe zisangalalo zili mkati, akadaulo achenjeza kuti kusangalala kopanda bajeti ndiko kumachititsa mwezi wa January kukhala wowawa kwa anthu ochuluka…
Read More » -
Adandaula za misewu yosakonzedwa
Pomwe anthu akhala akuitsotsombetsa nthambi ya Road Fund Administration ati ponena kuti ikukanika kukonza misewu ya m’dziko muno chonsecho nthambiyo…
Read More »