Nkhani
-
Akhazikitsa ndondomeko za CDF
Unduna wa maboma ang’onoang’ono wati makhonsolo ndi okonzeka kuyendetsa thumba la ndalama za chitukuko la CDF pogwiritsa ntchito ndondomeko zomwe…
Read More » -
Mlandu wa a Malemia ukupitirira mawali
Bwalo la milandu la Zomba Senior Resident Magistrates Court kuyambira 8 koloko mawa lino lipitiriza kumva mlandu wa a Senior…
Read More » -
Amalawi akufinyika
Pamene mtengo wa mafuta udakwera Lachitatu sabata ikuthayi, Amalawi ochokera m’madera osiyanasiyana m’dziko lino ati kulira n’kosayamba. Koma ikakuona litsiro…
Read More » -
Ana 63 mwa 100 akukwapulidwa
Makolo ena ati ndi wokondwa ndi mfundo yoti pakhale chilango chokhazikika kwa aphunzitsi amene angapezeke akumenya ophunzira. Komiti yoona za…
Read More » -
Afufuza zogulitsa Amaryllis Hotel
Nyumba ya Malamulo Lachiwiri lidayamba kufufuza momwe oyendetsa thumba la ndalama za penshoni za ogwira ntchito m’boma idagulira hotela ya…
Read More » -
Kampeni itha mawa
Pomwe Chisankho Chapadera chikuchitika m’madera a aphungu 4 ndi makhansala 9 Lachiwiri, kampeni yovomerezeka imene idayamba pa 15 January itha…
Read More » -
MRA ikuyendera nyumba za renti
Bungwe lotolera misonkho m’dziko lino la Malawi Revenue Authority (MRA) lati layamba kuyendera khomo ndi khomo anthu amene ali ndi…
Read More » -
Alangiza MEC isake njira yobweretsera mabaloti
Mkulu wa bungwe lolimbikitsa demokalase la Centre for Multiparty Democracy (CMD) a Boniface Chibwana aunikira bungwe la Malawi Electoral Commission…
Read More » -
‘Chuma chifike kumudzi’
Nduna ya za chuma a Joseph Mwanamvekha ati ndondomeko ya za chuma imene apereka m’Nyumba ya Malamulo dzulo ikuonetsetsa kuti…
Read More » -
Otsutsa aopseza kunyanyala zokambirana atamangidwa
Aphungu otsutsa boma ku Nyumba ya Malamulo aopseza kuti zomanga aphungu mwachisawawa zikapitirira iwo a zinyanyala ntchito za ku nyumbayo…
Read More »