Nkhani
-
A Mtsiro aiphula
Maumboni oyamikira a Ledson Mtsiro akuyenda ngati madzi m’masamba a mchezo pamene Amalawi 423 adasonkha pafupifupi K6.1 miliyoni powathokoza pa…
Read More » -
Akufuna kumanga nyumba zoteteza ofuna kudzipha
Bungwe la Azibambo Tibe Khonde Mental Health Initiative lati likufuna kukhala ndi malo 14 m’dziko la Malawi kumene anthu angakatule…
Read More » -
Mkokemkoke pa za maufumu
Pali mkokemkoke pakati pa maufumu a m’dziko lino ndi boma pa malire amene mbali ziwirizi zingatenge potsatira malamulo. Chikalata chimene…
Read More » -
Amalizitsa ntchito yosamutsa Amalawi ku Joni
Gulu lomwe lakhala likuthandiza anthu omwe adathawa m’nyumba zawo ndipo amakhala movutika kutsatira zipolowe zothotha anthu a maiko ena m’dziko…
Read More » -
‘Lamya zikadathandiza kafukufuku wa ndege’
Lamya za m’manja za omwe adali m’ndege ya asilikali a nkhondo yomwe idagwera ku Chikangawa zikadapezeka msanga n’kuchitidwa chipikisheni zidakatha…
Read More » -
Achenjeza maboma 23 za nyengo ya el nino
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yachenjeza kuti ulosi woyamba wa nyengo ya mvula ya chaka chino wasonyeza…
Read More » -
Ngozi za sitima zagundika
Kusowa kwa zizindikiro zosonyeza pomwe sitima ikudutsa, kugulitsa malonda mphepete mwa njanji ngakhalenso kufuna kudzipha, ndi zina mwa zimene zikukolezera…
Read More » -
‘Ikutrenda’ ndi Scorchers
Timu ya mpira wa miyendo ya atsikana ya Scorchers yagwedeza masamba a mchezo, inde kutrenda, pomwe yagometsa ambiri polowa mpikisano…
Read More » -
Alangiza aphungu achepetse tulo
Aphungu a ku Nyumba ya Malamulo adakwangula mkumano wawo sabata yatha atadutsitsa mabilu 14 omwe ambiri akukhudza za chuma ndi…
Read More » -
Amanga opezeka ndi mankhwala popanda chilolezo
Apolisi ku Mponela m’boma la Dowa amanga abambo atatu omwe adapezeka ndi mankhwala osiyanasiyana omwe amagulitsa mgolosale yawo. Mneneri wa…
Read More »