Nkhani

  • Chikho cha fodya chasefuka

    Chikho cha fodya chaka chino chasefukira ndi makilogalamu 27 miliyoni zomwe zabweretsa nkhawa yoti mtengo wake ukhoza kukhala wonyotsolera ku…

    Read More »
  •  Akhazikitsa ndondomeko za CDF

     Unduna wa maboma ang’onoang’ono wati makhonsolo ndi okonzeka kuyendetsa thumba la ndalama za chitukuko la CDF pogwiritsa ntchito ndondomeko zomwe…

    Read More »
  • Mlandu wa a Malemia ukupitirira mawali

    Bwalo la milandu la Zomba Senior Resident Magistrates Court kuyambira 8 koloko mawa lino lipitiriza kumva mlandu wa a Senior…

    Read More »
  •  Amalawi akufinyika

    Pamene mtengo wa mafuta udakwera Lachitatu sabata ikuthayi, Amalawi ochokera m’madera osiyanasiyana m’dziko lino ati kulira n’kosayamba. Koma ikakuona litsiro…

    Read More »
  • Ana 63 mwa 100 akukwapulidwa

    Makolo ena ati ndi wokondwa ndi mfundo yoti pakhale chilango chokhazikika kwa aphunzitsi amene angapezeke akumenya ophunzira. Komiti yoona za…

    Read More »
  • Afufuza zogulitsa Amaryllis Hotel

    Nyumba ya Malamulo Lachiwiri lidayamba kufufuza momwe oyendetsa thumba la ndalama za penshoni za ogwira ntchito m’boma idagulira hotela ya…

    Read More »
  • Kampeni itha mawa

    Pomwe Chisankho Chapadera chikuchitika m’madera a aphungu 4 ndi makhansala 9 Lachiwiri, kampeni yovomerezeka imene idayamba pa 15 January itha…

    Read More »
  • MRA ikuyendera nyumba za renti

    Bungwe lotolera misonkho m’dziko lino la Malawi Revenue Authority (MRA) lati layamba kuyendera khomo ndi khomo anthu amene ali ndi…

    Read More »
  • Alangiza MEC isake njira yobweretsera mabaloti

    Mkulu wa bungwe lolimbikitsa demokalase la Centre for Multiparty Democracy (CMD) a Boniface Chibwana aunikira bungwe la Malawi Electoral Commission…

    Read More »
  • ‘Chuma chifike kumudzi’

    Nduna ya za chuma a Joseph Mwanamvekha ati ndondomeko ya za chuma imene apereka m’Nyumba ya  Malamulo dzulo ikuonetsetsa kuti…

    Read More »
Back to top button