Nkhani
-
Fisi wadya mayi wa ku Tsangano
Anthu a m’mudzi mwa Doviko, Mfumu Mpando, m’boma la Ntcheu, akukhala ndi mantha chifukwa cha afisi omwe akuzunguza m’deralo. Loweruka…
Read More » -
Mzomera wadzipereka m’manja mwa apolisi
Gavanala wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) m’chigawo chakumpoto Christopher Mzomera Ngwira wadzipereka m’manja mwa apolisi Lachinayi. Mzomera, yemwe…
Read More » -
Kainja wadza ndi lumo lakuthwa
Mkulu wapolisi George Kainja wati adzutsa milandu yonse yogonera n’cholinga chopereka chikhulupiriro mwa Amalawi chokhudza apolisi. Pocheza ndi wailesi ya…
Read More » -
Chisale watuluka n’kumangidwanso
Mawu a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Klaus Chilima, womwe amauza anthu m’misonkhano yake ya kampeni kuti adzakwizinga…
Read More » -
Sipakala waimitsa Nyumba ya Malamulo
Sipikala waimitsa Nyumba ya Malamulo kwa sabata ziwiri kaamba ka phungu ndi ogwira ntchito ena ku nyumbayi omwe akhudzidwa ndi…
Read More » -
Chakwera akwanitse malonjezo—HRDC
Bungwe la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati maso ake akadali otsegula n’cholinga choti boma la Tonse Alliance lisaphwanye ufulu…
Read More » -
Masankhidwe a nduna autsa mapiri pa chigwa
Mtsutso wabuka ndi mmene mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus McCarthy Chakwera, wasankhira nduna za boma lake. Amalawi ena akuti sakuonapo…
Read More » -
Malonjezo ayamba kuoneka
Boma latsopano la Tonse Alliance layamba kukwaniritsa ena mwa malonjezo ake a panyengo ya kampeni ndipo pomwe akadaulo osiyanasiyana ayamikira…
Read More » -
Maudindo ayamba kuchucha m’boma
Pomwe mtsogoleri wa dziko lino yemwe wangosankhidwa kumene Lazarus Chakwera wayamba kusankha adindo m’bom, ku Nyumba ya Malamulo zinthu zasadabuzika.…
Read More » -
Takonzeka kuvota—Amalawi
Pamene kwangotsala masiku awiri kuti Amalawi 6.8 miliyoni aponye voti yosankha mtsogoleri wa dziko lino, Amalawi ena asonyeza chidwi kuti…
Read More »