Nkhani
-
182 adzipha mu sept
Chiwerengero cha anthu omwe akudzipha chikunka chikwera m’dziko muno. Kafukufuku amene Msangulutso adapanga akuonetsa kuti sipakutha sabata osamva nkhani kuti…
Read More » -
Chakwera, Nankhumwa akhambitsana
Chilinganizo chomwe chidaikidwa pofuna kuti mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera akayankhe mafunso m’Nyumba ya Malamulo chidasanduka mtsutso pakati pa…
Read More » -
Akwapula mphunzitsi wochita ‘chisembwere’
Maphunziro a ana a Sitandade 8, adasokonera Lolemba pasukulu ya pulaimale ya Kalira, yomwe ili m’mudzi mwa Kanyera ku Mtakataka…
Read More » -
Okalamba 46 aphedwa zaufiti
Anthu okalamba 36 adaphedwa pakati pa January ndi December 2019 pomwe ena 10 adaphedwa pakati pa January ndi September 2020…
Read More » -
Chakwera wakwera paphiri
Akadaulo osiyanasiyana ati Pulezidenti Lazarus Chakwera waonetsa chamuna popita ku Nyumba ya Malamulo kukayankha mafunso a aphungu pankhani zokhudza dziko…
Read More » -
Alimi alirira Admarc
Lipoti la nthambi yochenjeza anthu za njala ya Famine and Early Warning Network (FewsNet) lati alimi a chimanga akupitirira kulira…
Read More » -
Zotsamwitsa pa kutseguliranso sukulu
Pomwe ana asukulu akuyembekezera kutsegulira sukulu, aphunzitsi akuti sadakonzeke zokaphunzitsa chifukwa boma silikuonetsa chidwi pa nkhawa zawo. Mlembi wa bungwe…
Read More » -
Anthu sakudziteteza ku matenda a Covid-19
Ngakhale akadaulo azaumoyo adalosera kuti chiwerengero cha odwala Covid-19 chikwera kwambiri mwezi uno, anthu ambiri sakutsata njira zodzitetezera ku matendawa.…
Read More » -
Chloroquine sachiza Covid-19
Akatswiri azaumoyo atsutsa zoti chloroquine amachiza coronavirus. Akadaulowa amathirirapo ndemanga pa kanema yemwe anthu akugawana pa masamba awo a mchezo…
Read More » -
Ndale zimasokoneza ntchito zathu—MPS
Malawi Police Service (MPS) yavomera kuti mmbuyomu imalephera kugwira ntchito zawo mwaukadaulo kaamba ka andale omwe amalowerera kwambiri pa ntchito…
Read More »