Nkhani
-
Uladi akaseweza zaka 5
Khothi lalikulu ku Lilongwe Lachinayi lidagamula mkhalakale pandale Uladi Mussa kuti akasewenze zaka 5 pa mlandu wopotoza dala ntchito ya…
Read More » -
Uladi akaseweza zaka 5
Khothi lalikulu ku Lilongwe Lachinayi lidagamula mkhalakale pandale Uladi Mussa kuti akasewenze zaka 5 pa mlandu wopotoza dala ntchito ya…
Read More » -
Bajeti yadutsa, koma m’zikhomo
Nyumba ya Malamulo Lachitatu idavomereza bajeti ya K2.2 triliyoni ya chaka cha 2020 mpaka 2021 aphunguwo atayikambirana kuyambira Lolemba. Bajetiyo…
Read More » -
‘Chidodo pamilandu’
Mitima ya Amalawi yayamba kuwira ndi chidodo chomwe chikuchitika pa milandu ina yomwe akadaulo akuti ndi mlingo omwe Amalawiwo akugwiritsa…
Read More » -
Chakwera akumbukira masiku 100 a Tonse
Lolemba, mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera adali ndi mwambo wokumbukira kuti watha masiku 100 akulamula dziko lino. Pamwambo umene…
Read More » -
‘Amalawi dekhani’
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati Amalawi asayembekezere kuti zonse zomwe adalonjeza nthawi ya kampeni zingakwaniritsidwe nyengo yochepa chifukwa…
Read More » -
Aphunzitsi akhala ndi khonsolo
Unduna wa za maphunziro wati ukufuna kukhazikitsa khonsolo ya aphunzitsi yoti izikhazikitsa mwambo komanso kutukula ntchito yauphunzitsi. Nduna ya za…
Read More » -
Akumba manda m’khonde la nyumba
Athu okwiya aika maliro pakhomo pa mkulu wina ku Chirimba mumzinda wa Blantyre yemwe amamanga nyumba panjira yolunjika kuchipata cha…
Read More » -
Aphungu akana makondomu aulere
Aphungu a Nyumba ya Malamulo Lachitatu adabweza mphatso ya makondomu 206 000 yomwe bungwe la Aids Health Foundation (AHF) lidapereka…
Read More » -
Takana kupha makanda
Ife sitivomera kupha makanda.” Uwu ndi uthenga womwe aphungu a Nyumba ya Malamulo auza Tamvani kuti aombera bilo yopatsa mwayi…
Read More »