Nkhani
-
Ndale zosadula chitukuko zikhumudwitsa aMalawi
Kudula ntchito zimene adayambitsa atsogoleri akale a dziko lino kukuchititsa kuti Amalawi azingosaukirabe chifukwa ndalama zambiri zimangolowa m’madzi ntchitozo osamalizidwa.…
Read More » -
Wa zaka 22 akufuna uphungu
Timamva kuti achinyamata ndi atsogoleri a mawa, koma msungwana wa zaka 22 ku Nsanje wati akufuna kudzaimira chipani cha PP…
Read More » -
Escom isayerekeze kukweza magetsi—Banda
Kutsatira zomwe mkulu wa zachuma kukampani ya magetsi m’dziko muno ya Escom Delano Ulanje adauza wailesi ya MBC kuti bungweli…
Read More » -
Kanduku achotsa mfumu
Kwathina ku Mwanza pamene T/A Kanduku wachotsa gulupu Thambala komanso kulamula ena awiri kuti alipe mbuzi. Bwanamkubwa wa bomalo Gift…
Read More » -
Escom, ganizirani Amalawi
Utsi sufuka popanda moto. Mwambiwu umatanthauza kuti kalikonse kamveka sikatero pachabe. Zamveka kuti bungwe la Escom likufuna kukweza magetsi, tikukhulupirira…
Read More » -
Amayi tizivulana tokhatokha?
Pali zinthu zina zoti mnzako akachita owonawe umazizwa, kuchita kakasi kuti kodi winayo waganiza bwanji? Mwachitsanzo, pali zakudya zina zoti…
Read More » -
Flames ikaluza, Tom abwerera?
Kuli nkhondo ku Calabar lero. Flames ikhala ikuphana ndi Nigeria masewero amenenso aunikire ntchito ya mphunzitsi wa Flames Tom Saintfiet.…
Read More » -
Lundu, Kaomba apita ku mwambo wa Kulamba?
Mafumu aakulu a Achewa muno m’Malawi Paramount Chief Lundu ndi Senior Chief Kaomba, akana kunena ngati apite kumwambo wa Kulamba…
Read More » -
Adzudzula JB zomanga mfumu
Mphunzitsi wa za malamulo kusukulu yaukachenjede ya Chancellor College Mwiza Nkhata wati ndi zodabwitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino Joyce…
Read More » -
Mafumu aluzanitse mtundu
Nthawi ya mwambo wa Achewa wa Kulamba yafikanso. Paja chikhalidwe ndiye mizu ya mtundu ulionse. Achewa amasonkhana malo amodzi monga…
Read More »