Nkhani
-
Love ya pa Zed ikutipweteka
La 40 lakwana. Zochitika ku Zambia komwe Flames imakapikisana nawo mumpikisano wa Cosafa zadziwika. Kumeneko Flames idataya bomwetamweta koma ati…
Read More » -
Tikulumirabe ana chakudya?
Masiku ano pomwe matenda a Edzi afala mwa nkhani nkhani pakufunika kuonetsetsa komanso kusintha zinthu zina zomwe anthu timachita makamaka…
Read More » -
MCP yatiphunzitsa zambiri
Nkhani idali mkamwamkamwa miyezi ingapo yapitayi ndi ya msonkhano waukulu wa chipani cha MCP. Zimakaikitsa ngati kumsonkhanowo kukamangidwe mfundo zolemekeza…
Read More » -
Apereka ambulansi ku Bangwe
Kwa kanthawi anthu makamaka amayi oyembekezera akhala akuvutika mayendedwe popita ku chipatala cha Bangwe Clinic mumzinda wa Blantyre. Anthu omwe…
Read More » -
Tom sakufunanso ndalama?
Kati deru kadazizwitsa mlenje. Ife aganyu tadzidzimuka ndi ganizo la mphunzitsi wa Flames Tom Saintfiet yemwe tsopano wanena kuti sakufunanso…
Read More » -
Za mahedifoni pamsewu
Malinga ndi kupita patsogolo kwa zipangizo zogwiritsa ntchito pamoyo wa tsiku ndi tsiku, makhalidwe ndi zochita za anthu zikusinthanso. Pafupifupi…
Read More » -
‘Sibwino kulekeza panjira kumwa ma ARV’
Mmodzi mwa anthu amene adapezeka ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ndipo akukangalika kuphunzitsa ena za matendawa Hannah Mandanda wati…
Read More » -
Pepa Gaba, Malata
Chalaka bakha nkhuku siyingatole. Nkhani ya Gabadinho Mhango ndi Lucky Malata ndiyo yatinenetsa mwambiwu. M’sabatayi nkhani idawawasa ndi ya anyamatawa…
Read More » -
Sinodi ya Nkhoma ikudana ndi zochotsa mimba
Sinodi ya Nkhoma ya mpingo wa CCAP yati kuloleza kuti amayi azichotsa mimba ndi kolakwika, nkhanza, uchimo komanso usatana pamaso…
Read More » -
‘Ndale zachibwana zalowa ku MCP’
Kadaulo wa ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College Blessings Chinsinga wati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chalowa chibwana,…
Read More »