Chichewa
-
Moto buuu! 2019 yafukiza zipani
Fumbi lachita kobooo! m’zipani pamene kwangotsala chaka chimodzi kuti chisankho cha patatu chichitike m’dziko muno. Chisankho cha patatu chidzakhalako pa…
Read More » -
Akufuna boma likweze malipiro
Bungwe loona za ufulu wa anthu ogwira ntchito la Malawi Congress of Trade Union (MCTU) lapempha boma kuti likweze mlingo…
Read More » -
Apayoniya akana zionetsero
Amene adali a Malawi Young Pioneers (MYP) omwe atha miyezi 10 akubindikira ku Lilongwe kufuna ndalama zawo zopumira pantchito ndipo…
Read More » -
Amalawi alankhula: Masiku 30, boma liyankhe—Gift Trapence
Malawi adayaka moto dzulo m’zigawo zonse pamene anthu adayenda pokhumudwa ndi ntchito za boma la DPP. Mfundo yamangidwa ndiyoti boma…
Read More » -
‘Mundibwezere voti yanga’, amalawi athafulira APM pazionetsero
Amalawi athera Chichewa mtsogoleri wa dziko lino komanso nduna zake pa zionetsero zomwe zidachitika Lachisau. Zionetserozo zidatsogoleredwa ndi amipingo, amabungwe…
Read More » -
Wopha Wame akasewenza moyo wake wonse
Bwalo la milandu lalikulu m’boma la Salima Lachitatu lidagamula Limbani Maliro, mnyamata yemwe adapha Mlaliki Shadreck Wame kukasewenza moyo wake…
Read More » -
‘Kusintha lamulo la ufiti kwachedwa udyo’
Kuchedwa kwa ntchito yosintha lamulo lokhudza zaufiti kukuchititsa kuti okalamba amene akuwaganizira kuti ndi mfiti apitirire kuzunzidwa komanso kuphedwa, atero…
Read More » -
Adindo akhudzidwa pa imfa ya Masambuka
Kusowa kwa mnyamata wa chialubino m’boma la Machinga kwavumbulutsa zinthu zoziritsa thupi. Macdonald Masambuka wa zaka 22 yemwe ankachokera…
Read More » -
Dipo la chithyolakhola limawawa pazovuta
Munthu akakwatira mkazi mongozemba osatsata ndondomeko amati wathyola khola. Nthawi ikafika yoti munthu otere alongosole banja, amalipitsidwa madipo osiyanasiyana kwa…
Read More » -
Madzi achita thope ku DPP
Madzi sakudikha kuchipani cha DPP pamene mpungwepungwe wolimbirana amene adzatsogolere chipanichi ku chisankho cha 2019 wafika pa kamuthemuthe.…
Read More »