Chichewa
-
Mangani womenya wotsatira MCP
Chipani chotsutsa cha MCP chapempha apolisi kuti aponye m’chitokosi Isaac Jomo Osman, kadeti wa DPP amene adasautsa ndi kuvulitsa mnyamata…
Read More » -
Chilima saima nawo
Uli dere n’kulinga utayenda naye. Amene akufuna kuti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima adzaimire chipanicho pachisankho cha…
Read More » -
Ndikakunyenyani kukovenshoni—APM
Pamene chipani cha DPP chalengeza kuti msonkhano waukulu ulipo mwezi wa mawa, mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika Lachinayi adati…
Read More » -
Chipatala chidzapulumutsa K730m pachaka
Chipatala cha khansa chomwe boma likumanga ku Lilongwe chikatsegulidwa mwezi wa September chaka chino, boma kudzera ku Unduna wa Zaumoyo…
Read More » -
Mswahara wa zifukwa
Munga wadza ndi mafinya omwe. Pamene ena akumwetulira kuti boma lakweza mswahara wa mafumu, mafumu ena ati kukwezaku kuwabweretsera mavuto…
Read More » -
‘Lingalirani bwino musanathane ndi fodya’
Akatswiri komanso alimi ati dziko la Malawi likuyenera kulingalira mozama lisadagonjere khumbo la bungwe la zaumoyo padziko lonse la World…
Read More » -
Palibe mlendo ku MCP—Munthali
Pomwe chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chidachititsa msonkhano wake waukulu kumathero a sabata yapitayi mwa mpanimpani pothawa ziletso ku…
Read More » -
‘Chilonda chatukusira mu DPP’
Bwerani poyera mulankhule kwa Amalawi. Awa ndi mawu a akadaulo pa ndale pamene alangiza mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika…
Read More » -
New grain technology excites govt
The Ministry of Agriculture, Irrigation and Water Development has challenged innovators to come up with more technologies aimed at cutting…
Read More » -
Wopanda chiphaso cha nzika sadzavota—MEC
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latsimikiza kuti chiphaso chakale chovotera sichidzanunkha kanthu pachisankho cha 2019. Wapampando wa…
Read More »