Chichewa
-
Zipani za moyo zioneke—CMD
Kodi zipani zinazi zili moyo? Nthawi yofukula yakwana m’zipani pamene bungwe loona mgwirizano wa zipani zosiyanasiyana la Centre for…
Read More » -
Samalani ndi sikelo za chinyengo—MBS
Nthawi yokolola yakwana, pomwe alimi amataya zokolola zawo kwa mavenda akuba amene amamanga sikelo pofuna kuliza alimi. Koma bungwe loona…
Read More » -
Ambwandira msilikali ku Salima
Apolisi a chigawo chapakati abatha msilikali wa nkhondo ndi anthu ena awiri powaganizira kuti adapezeka ndi chamba popanda chilolezo. Msilikaliyu,…
Read More » -
Chipatala cha khansa chitheka September
Odwala khansa ayembekezere kupuma umoyo wina. Chipatala chachikulu chothana ndi matendawa chitsegulidwa September chaka chino mumzinda wa Lilongwe. Nduna ya…
Read More » -
Akupopa zimbudzi pochepetsa matenda
Ena zimbudzi zawo zikadzadza amagwetsa ndi kukumba china. Uku ndi kutha malo. Lero zinasintha chifukwa khonsolo ya Blantyre mogwirizana ndi…
Read More » -
Kuli ziii! Pa za mthandizi
Kwangoti zii! Nkhawa yagunda ngati ntchito za mthandizi zomwe anthu amalandira kangachepe akalima msewu ichitike popeza nthawi yake yadutsa osamvapo…
Read More » -
Anatchereza
Mkazi wanga koma mkonono Agogo, Langa ndi dandaulo pa mkazi wanga wokondeka. Iyetu mwano alibe ndiponso ntchito amagwira molimbika. Abale…
Read More » -
Kukuza ziwalo kwabooka
Masiku ano ukatsegula wailesi kapena nyuzipepala ngakhalenso poyenda mphepepete mwa msewu ngakhalenso m’malo modikirira mabasi, uthenga omwe watenga malo ndi…
Read More » -
Akwizinga ‘wogwirira’ wamisala
Apolisi ya Kanengo ku Lilongwe anjata bambo wa zaka 46 Nelson Chiudzu pomuganizira kuti adagwirira mai wa zaka 49…
Read More » -
‘Tidadziwana tili ana’
Mtolankhani wa za masewero ku wailesi ya Voice of Livingstonia (VOL) Sylvester Siloh Kapondera adakumana ndi wokondedwa wake Annie Chivunga…
Read More »