Chichewa
-
Mphekesera zizunza anthu ku Mangochi
Zina ukamva, kamba anga mwala ndithu. Anthu a m’boma la Mangochi sabata yapitayi adadzuka pakati pausiku, ena m’bandakucha, n’kuyamba kukupa…
Read More » -
A Malawi akufuna 2018 wa ngwiro
Pomwe chaka cha 2018 changoyamba kumene, mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma Lazarus Chakwera ndi akadaulo ena ati boma lisinthe kayendetsedwe…
Read More » -
‘ankawerenga nkhani pa mij’
Ndi mawu okha, MarcFarlane Mbewe wa Capital Radio adachiritsidwa. Awa ndi makumanidwe a mnyamatayu ndi Lisa Lamya, mtolankhani wa Yoneco…
Read More » -
Ndewu ya gule kudambwe
Kudali fumbi koboo! Kudambwe la Phingo m’boma la Chikwawa pamene gulewamkulu adaponyerana zibakera pokanganirana zovala zovinira. Mneneri wapolisi ya Chikwawa…
Read More » -
‘Osalanga nokha oganiziridwa ufiti’—Apolisi
Anthu m’mudzi mwa Chimchembere kwa T/A Chekucheku m’boma la Neno adavomera mwa mphamvu kuti ufiti ulipo, makamaka mphenzi zopanga anthu.…
Read More » -
Kuli zionetsero pa 13 December
Lachitatu pa 13 December kukhala ali ndi mwana agwiritse m’zigawo zonse zitatu za dziko lino pamene bungwe la mipingo la…
Read More » -
‘Mafumu adyera’
Akatswiri pandale komanso mafumu adzudzula zomwe adachita mafumu ena poyenda ndawala ulendo ku Nyumba ya Malamulo komwe amakatsutsa mabilo a…
Read More » -
Rasta akaseweza zaka 6
Mlandu woba njinga komanso kulasa ndi mpeni paphuzi pa bambo wa kabaza, watumiza Fedson Missi kundende komwe akaseweze zaka 6.…
Read More » -
Malawi ali mu mdima
Zasokonekera! Malawi ali pamoto wosaneneka ndi kuzimazima kwa magetsi. Anthu akumudzi akugona kuchigayo kudikira magetsi pamene alimi a ng’ombe zamkaka…
Read More » -
‘Timakaonera masewero a mpira’
Masewero a pakati pa Police Secondary School ndi St Paul Private Secondary ku Zomba adzakhala chikumbutso kwa Owen Chaima, kuti…
Read More »