Chichewa
-
Malawi ali mumdima wa dzaoneni
Dziko la Malawi laona mdima womwe sudaonekepo chilandirireni ufulu wodziyimira palokha. Madera ena akukhala masiku awiri magetsi osayaka. Kwina, ndiye…
Read More » -
Pac iwopseza boma pa bilo yachisankho
Lisafike Lachitatu sabata ya mawa musanabweretse bilo yokhudza chisankho ndi maboma ang’ono. Latero bungwe la amipingo la Public Affairs Committee…
Read More » -
Matafale memorial shows under threat
It is Wednesday. Four days before the annual Evison Matafale Memorial Show in Blantyre. But the Black Missionaries are yet…
Read More » -
Zipani zikufuna mayankho pa zitupa za unzika
Zipani za Malawi Congress Party (MCP) ndi People’s Party (PP) zati kusowa kwa zitupa zina za olembetsa m’kaundula wa unzika…
Read More » -
Zitupa zaunzika zina zasowa
Zitupa 93 893 za uzika m’boma la Kasungu zasowa. Tamvani itha kuvumbulutsa. Izitu zadziwika pamene bungwe lolembera unzika la National…
Read More » -
Achita zionetsero za kuthimathima kwa magetsi
Anthu okhudzidwa a mu mzinda wa Lilongwe adachita ziwonetsero zosonyeza kukwiya kwawo ndi kuthimathima kwa magetsi m’dziko muno. Cholinga cha…
Read More » -
‘Boma likutengera a Malawi kumtoso’
Pamene nkhani ya malamulo oyendetsera zisankho ili mkamwamkamwa, mkulu womenyera ufulu wa anthu, John Kapito, wati nkhani za magetsi, madzi…
Read More » -
Titsirika nkhalango zonse—Ng’anga
Gulu lina la asing’anga ku Dedza ladzithemba kuti likhoza kuteteza nkhalango za dziko lino ndi chambu koma akuluakulu a boma…
Read More » -
Makuponi n’chipsinjo—Mafumu
Kuchepa kwa makuponi ogulira zipangizo za ulimi zotsika mtengo omwe boma limagawa kwa anthu mogwirizana ndi mafumu, kukubweretsa chitonzo kwa…
Read More » -
Tambala wameza chimanga
Kusadabuzika kwa chipani cha DPP pa chisankho chapadera kukutanthauza kuti Amalawi atopa ndi ulamuliro wa chipanicho, akadaulo a ndale ena…
Read More »