Chichewa
-
Chitetezo chaphwasuka
Chitetezo chaphwasuka. Anthu akuberedwa, kumenyedwa ndi kuchitidwa zachipongwe zambiri. Akaitanitsa apolisi akuti akumatenga nthawi kuti abwera ndipo nthawi zina sabwera.…
Read More » -
Kolera yaluma mano
Nthenda ya kolera imene idayamba ngati njerengo mwezi wa November chaka chatha, ikukwererabe moti kuchoka Lachisanu sabata yatha chiwerengero…
Read More » -
Kalembera wa mafoni aima
Boma laimitsa kalembera wa lamya za m’manja yemwe nthambi yoyendetsa ntchito za mauthenga ya Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) idakhazikitsa…
Read More » -
Chilimikani pa ulimi—Kazembe
Malinga ndi ng’amba imene yasautsa m’madera ambiri m’dziko lino, wachiwiri kwa kazembe wa limodzi mwa maiko a ku Ulaya la…
Read More » -
MEC ikufunakusinthatsiku la chisankho
Pavuta kuti chisankho chichoke mwezi wa May kupita September monga bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lidapemphera komitiya…
Read More » -
Osinthasintha zipani ngosadalilika—Akadaulo
Andale osinthasintha zipani ndi osadalilika, ndipo amachita izi chifukwa cha dyera, atero akadaulo ena a zandale. Koma ena mwa andalewo…
Read More » -
Kwadza kaundula wa foni za m’manja
Eni lamya za m’manja m’dziko muno akuyenera kulowa m’kaundula wa umwini wa lamya zawo kuti azitha kugwiritsa ntchito lamya zawozo,…
Read More » -
NRB ionjezera masiku otengera zitupa
Ntchito yopereka zitupa za unzika kwa anthu a m’maboma 15 m’dziko muno, imene imayenera kutha dzulo ayionjezera m’boma la Blantyre,…
Read More » -
Achenjeza zipani
Akadaulo a zandale ena ati zomwe akuchita akuluakulu a zipani polekelera kukokanakokana m’zipani zawo n’kutsekeleza mwayi wodzapambana pachisankho cha 2019.…
Read More » -
Apolisi, mabungwe akufuna kuteteza ufulu wa ana
Apolisi ati agwirana manja ndi mabungwe osiyanasiyana pa ntchito yoteteza ufulu wa ana m’dziko muno. Mkulu wa polisi ya Chirimba,…
Read More »