Chichewa
-
Amalawi apindulanji ndi kutsogolera Sadc
Akuluakulu pa zachuma komanso mafumu m’dziko muno ati mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda afunika masomphenya kuti dziko lino lipindule…
Read More » -
Amalawi apindulanji?
Sabata yatha mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda adakhala wapampando wa bungwe la mgwirizano wa maiko a kumwera kwa Africa…
Read More » -
Kusiya ana akunjira muwilo
Sabata yathayi mmodzi wa awerengi a tsambali adafunsapo pankhani ya ana akunjira, makamaka mounikirapo pa zikalata zomwe makolo owabereka amasiya…
Read More » -
Chikho cha Carlsberg chafika pachimake
Thambo lagwa, chikho cha Carlsberg chaka chino chabwera ndi zake pamene anyamata ovala jombo atenga malo kugwedula matimu omwe amakula…
Read More » -
Chakwera angadze ndi kalumo kakuthwa
Mlendo ndiye adza ndi kalumo kakuthwa. Akadaulo pandale ati kusankhidwa kwa mbusa Dr Lazarus Chakwera kukhala mtsogoleri wa chipani chachikulu…
Read More » -
Aika mwala wa maziko kawiri pachipatala
Lolemba m’sabatayi mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda adatsogolera anthu a m’boma la Ntcheu pomwe amayala mwala wa maziko pa…
Read More » -
Love ya pa Zed ikutipweteka
La 40 lakwana. Zochitika ku Zambia komwe Flames imakapikisana nawo mumpikisano wa Cosafa zadziwika. Kumeneko Flames idataya bomwetamweta koma ati…
Read More » -
Tikulumirabe ana chakudya?
Masiku ano pomwe matenda a Edzi afala mwa nkhani nkhani pakufunika kuonetsetsa komanso kusintha zinthu zina zomwe anthu timachita makamaka…
Read More » -
MCP yatiphunzitsa zambiri
Nkhani idali mkamwamkamwa miyezi ingapo yapitayi ndi ya msonkhano waukulu wa chipani cha MCP. Zimakaikitsa ngati kumsonkhanowo kukamangidwe mfundo zolemekeza…
Read More » -
Apereka ambulansi ku Bangwe
Kwa kanthawi anthu makamaka amayi oyembekezera akhala akuvutika mayendedwe popita ku chipatala cha Bangwe Clinic mumzinda wa Blantyre. Anthu omwe…
Read More »