Chichewa
-
Tom sakufunanso ndalama?
Kati deru kadazizwitsa mlenje. Ife aganyu tadzidzimuka ndi ganizo la mphunzitsi wa Flames Tom Saintfiet yemwe tsopano wanena kuti sakufunanso…
Read More » -
Za mahedifoni pamsewu
Malinga ndi kupita patsogolo kwa zipangizo zogwiritsa ntchito pamoyo wa tsiku ndi tsiku, makhalidwe ndi zochita za anthu zikusinthanso. Pafupifupi…
Read More » -
‘Sibwino kulekeza panjira kumwa ma ARV’
Mmodzi mwa anthu amene adapezeka ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ndipo akukangalika kuphunzitsa ena za matendawa Hannah Mandanda wati…
Read More » -
Pepa Gaba, Malata
Chalaka bakha nkhuku siyingatole. Nkhani ya Gabadinho Mhango ndi Lucky Malata ndiyo yatinenetsa mwambiwu. M’sabatayi nkhani idawawasa ndi ya anyamatawa…
Read More » -
Sinodi ya Nkhoma ikudana ndi zochotsa mimba
Sinodi ya Nkhoma ya mpingo wa CCAP yati kuloleza kuti amayi azichotsa mimba ndi kolakwika, nkhanza, uchimo komanso usatana pamaso…
Read More » -
‘Ndale zachibwana zalowa ku MCP’
Kadaulo wa ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College Blessings Chinsinga wati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chalowa chibwana,…
Read More » -
Ulemu ulibe mkazi kaya mwamuna
Ulemu ndi khalidwe lofunika pamoyo wa munthu wina aliyense—wamwamuna kapena wamkazi—choncho mtsogoleri wadziko lino sadaphonye kwenikweni masiku apitawa pomwe adakumbutsa…
Read More » -
Joyce Banda akumana ndi mafumu, otsutsa azizwa
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda Lachinayi adakumana ndi mafumu a m’dziko muno, zomwe zidachititsa otsutsa boma ena kuzizwa. Banda…
Read More » -
Kaundula wa mavoti akuyenda bwino
A Malawi m’madera ena adakhamukira kumalo olembetsa maina awo m’kaundula wa chisankho cha pa 20 May 2014. Malinga ndi mphunzitsi…
Read More » -
‘Chihana abweretse umboni za chuma cha Bingu’
Chipani cha DPP chati Yeremiah Chihana, amene adavumbulutsa zoti mtsogoleri wakale wa dziko lino Bingu wa Mutharika adali ndi chuma…
Read More »