Chichewa
-
Kanduku achotsa mfumu
Kwathina ku Mwanza pamene T/A Kanduku wachotsa gulupu Thambala komanso kulamula ena awiri kuti alipe mbuzi. Bwanamkubwa wa bomalo Gift…
Read More » -
Escom, ganizirani Amalawi
Utsi sufuka popanda moto. Mwambiwu umatanthauza kuti kalikonse kamveka sikatero pachabe. Zamveka kuti bungwe la Escom likufuna kukweza magetsi, tikukhulupirira…
Read More » -
Amayi tizivulana tokhatokha?
Pali zinthu zina zoti mnzako akachita owonawe umazizwa, kuchita kakasi kuti kodi winayo waganiza bwanji? Mwachitsanzo, pali zakudya zina zoti…
Read More » -
Flames ikaluza, Tom abwerera?
Kuli nkhondo ku Calabar lero. Flames ikhala ikuphana ndi Nigeria masewero amenenso aunikire ntchito ya mphunzitsi wa Flames Tom Saintfiet.…
Read More » -
Lundu, Kaomba apita ku mwambo wa Kulamba?
Mafumu aakulu a Achewa muno m’Malawi Paramount Chief Lundu ndi Senior Chief Kaomba, akana kunena ngati apite kumwambo wa Kulamba…
Read More » -
Adzudzula JB zomanga mfumu
Mphunzitsi wa za malamulo kusukulu yaukachenjede ya Chancellor College Mwiza Nkhata wati ndi zodabwitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino Joyce…
Read More » -
Mafumu aluzanitse mtundu
Nthawi ya mwambo wa Achewa wa Kulamba yafikanso. Paja chikhalidwe ndiye mizu ya mtundu ulionse. Achewa amasonkhana malo amodzi monga…
Read More » -
Amayi chepetsani zotsirana phalazi
Kawirikawiri nkhani ya nkhanza za m’mbanja imagonera abambo kuti ndiwo ali patsogolo kuzunza amayi. Tikaonetsetsa chiwerengero cha nkhanza za m’banja…
Read More » -
Za pasipoti ya Gaba sizikumveka
Sabatayi yakhala yomvetsa mutu ndi nkhani ya Gabadihno Mhango. Zachitika m’sabatayi aganyu zatiwawa ndipo tikufuna bungwe la FAM komanso timu…
Read More » -
Jombo ikudiliza matimu
Chalaka bakha nkhuku singatole. Linda madzi apite ndiye udziti wadala. Miyambiyi ndiyo idatsanuka m’sabatayi kaamba ka jombo yomwe idathudzula Nyerere…
Read More »