Chichewa
-
Chilengedwe chibwerere ku Mwanza
Mapiri, nkhalango komanso madambo ali mbulanda. Anthu adagwetsa mitengo ndi kuotcha makala. Koma lero nkhani yasintha. Pang’onopang’ono boma la…
Read More » -
Chenjerani, 2017 tisatuwe ndi njala’
Lero ndi tsiku lakutha kwa chaka cha 2016. Pomwe masiku athera kuchitseko ndipo chaka cha 2017 chili pamphuno, akadaulo…
Read More » -
Kupewa kutsegula m’mimba
Nthenda ya kutsegula m’mimba ndi imodzi mwa matenda omwe amakonda kufala kwambiri m’nyengo ino ya mvula. Malinga…
Read More » -
Milandu mbweee! mu 2016
Chapita chaka cha 2016 chomwe dziko lino lidaona ina mwa milandu ikuluikulu ikulowa m’mabwalo a milandu ndi kuweruzidwa. Umodzi mwa…
Read More » -
Tsala bwino 2016
Pamene tikutsendera chaka cha 2016, akadaulo ena pandale ati zochitika m’chakachi zikutsimikiza kuti Amalawi akuchenjera ndiye andale asamale mu…
Read More » -
Ulangizi paulimi mu 2016
Pamene tikulowa chaka chino mawa lino, ndi bwino tisanthule zina mwa nkhani zikuluzikulu komanso magawo amene tidakupatsirani mu Uchikumbe mu…
Read More » -
‘Tidasala masiku 52 kuti Mulungu atiunikire’
Nthawi zambiri, anthu timatenga banja ngati sitepe pamoyo wathu basi koma tikalingalira momwe banja la m’busa komanso mlembi wa mkulu…
Read More » -
Khirisimasi ya Niko
Nthawi ija yafikanso. Niko adali pa Wenela tsiku limenelo Abale anzanga, ndikuthokoza Mulungu amene wandilola kuti ndifike tsiku la…
Read More » -
Anatchezera
Za Chikondi ndi chibwenzi Agogo, Kodi chibwenzi ndi chikondi ndi zosiyana bwanji? Mwina funso limeneli likhoza kuoneka ngati lopanda nzeru…
Read More » -
Sankhani Mkandawire kulavula moto
Sankhani ‘Mkango Plus’ Mkandawire adachoka ku Nyasa Big Bullets chaka chino kupita ku Tanzania komwe akusewera Mbeya FC. Iye…
Read More » -
Afisi a ku ntcheu abwereranso?
MAyi adaphedwa, ana ake anayi ndi mlamu wake adavulazidwa. Pano ziweto 10 zagwidwa m’midzi 14 ya mwa T/A Phambala…
Read More » -
Fodya wobwerera kumsika amugulitsa
Mkulu wa bungwe la Tobacco Association of Malawi (Tama), Graham Kunimba, wati fodya yemwe anabwerera pamsika chaka chino tsopano amugulitsa.…
Read More » -
Atenge basi ndani?
Matimu a Nyasa Big Bullets ndi Mighty Be Forward Wanderers Lolemba akhala akukumana pampikisano wa Basi Ipite Soccer Fiesta wolimbirana…
Read More » -
‘Chisangalalo chafika, Samalani kuli mavuto’
Mawa laliwisiri ndi tsiku la Khirisimasi ndipo Lamulungu sabata ya mawa ndi tsiku lokumbukira kulowa chaka cha 2017. Iyi ndi…
Read More » -
‘Pewani ngozi, kuberedwa’
Nyengo ya Khirisimasi ndi Nyuwere kumachuluka ngozi za pamsewu, mchitidwe wa umbava ndi umbanda komanso ngozi zina monga kumira m’madzi…
Read More » -
Ma Queens ndi mphatso
Lolemba lapitali, mafumukazi athu, ma Queens, adali ku nyumba yachifumu ya Sanjika mumzinda wa Blantyre kumene mtsogoleri wadziko lino Peter…
Read More » -
Agumula nyumba pokaikira masalamusi
Mbuto ya kalulu idakula ntadzaonani. Mwambiwu udapherezera Lachiwiri ku Lilongwe pomwe anthu okwiya ku Mtsiriza adagumula nyumba ya banja lina…
Read More » -
Malingaliro a Khirisimasi
Khirisimasi ndi Januwale Zalowa m’manyumba (adalakwitsa ndi oimbayo osati in Tadeyo) Zaseseratu! Kwa amene adaliko nthawi imene Kennedy Ndoya, ankatchuka…
Read More » -
Anachezera
Zidatheka! Zikomo Anatchereza, Ndafuna ndikuthokozeni kwambiri chifukwa cha malangizo anu. Pano tidamanga banja ndi mtsikana wa ku Machinga uja ndipo…
Read More » -
‘Ngozi idazamitsa chikondi chathu’
Anthu adavulala, ena adataya miyoyo yawo. Koma kwa Joseph Chirwa ndi Towera udali mwayi kuti awiriwa akumane ndi kumanga woyera.…
Read More »