Chichewa
-
Akufuna mayankho pa njala ya m’zipatala
Mabungwe omwe si aboma ku Rumphi ati akudikirabe yankho kuchokera kwa mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika pa zakusowa…
Read More » -
Ana achoke m’minda—Nduna
Mvula yagwa Madera ambiri moti anthu ali kalikiriki m’minda kuthira manyowa, kubzala ndi kuwokera koma nkhawa yaikulu yagona pamchitidwe…
Read More » -
Alimi musaiwale mitengo ya chonde
Bungwe lomwe limalimbikitsa alimi kubzala mitengo yosiyanasiyana la World Agroforesry Centre lapempha alimi kuti asaiwale mitengo ya chonde akamabzala…
Read More » -
Ndi Walter, Mijiga Kapena Yabwanya?
Atatsatsa mfundo zawo masiku apitawa, omwe akulimbirana maudindo kubungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo la Football Association of…
Read More » -
Kamatira: Nthenda yosautsa
Thenda zina ukazimva mmakutu kuchita kuwawa chifukwa chakuwopsa kwake. Anthu ambiri amataya mtima ndi matenda aja a Edzi komatu…
Read More » -
‘Olandira makuponi pano mu 2016 sadzalandiranso’
Boma lati kuyambira chaka chino, yemwe wapindula nawo mupologalamu ya zipangizo zaulimi zotsika mtengo ya Farm Input Subsidy Programme…
Read More » -
Akupha makwacha ndi zipatso
Chaima Banda, mlimi wa zipatso kwa Manondo, T/A Nkukula ku Lilongwe, akusimba lokoma ndi ulimi wake womwe wakhala akuchita…
Read More » -
Anatchezera
Ndimukhulupirirebe? Agogo, Ndili pachibwenzi ndi mtsikana wina wake ndipo ndakhala naye mwezi umodzi. Vuto ndi loti iye ali ndi mimba…
Read More » -
Akumanga mvula ndani?
Tsikulo pa Wenela padali kutentha osati masewera. Zimachita kukhala ngati dziko likutha, Jahena akutsikira pansi pompano. N’chifukwa khamu lidafika apo…
Read More » -
Kasambara: Akhazikitsa chimbale mwezi uno
Martha Kasambala ndi woimba nyimbo zauzimu ndipo amakhala ku Mzuzu. Iye ali ndi zimbale ziwiri ndipo mu December muno akuti…
Read More » -
Atentha nyumba kaamba ka K2 000
Mkulu wina ku Ntchisi waona mbwadza atagamulidwa kuti akaseweze zaka 8 kundende kaamba kobutsa nyumba ya mnzake chifukwa cha…
Read More » -
Wagolosale ndiye adandipatsa nambala yake’
Anthuni, njira zophera khoswe n’zambiri koma chachikulu khosweyo afe basi. Ena pofuna mkazi amachita kugwa m’ngongole kuti aoneke ngati,…
Read More » -
Wofuna kugulitsa alubino achimina
Bwalo la milandu la Mzuzu majisitireti lalamula Philip Ngulube, wa zaka 21, kuti akakhale kundende ndi kukagwira ntchito yakalavulagaga kwa…
Read More » -
GANIZO LOKWEZA FIZI LIBWERETSA NJIRIMBA
Kudali matatalazi ku Nyumba ya Malamulo Lachinayi lapitali pamene aphungu adapindirana ndevu mkamwa pokambirana za ganizo la boma miyezi…
Read More » -
Za ukamberembere mu Fisp akuti zichepe chaka chino
Ntchito yotumiza zipangizo zaulimi zotsika mtengo mupologalamu ya Farm Input Subsidy Programme (Fisp) ili mkati koma nyengo ngati iyi…
Read More » -
Ku Nkhoma sakugona ndi mthirira
Amati mmera mpoyamba. Ukalephera kukonzekera koyambirira ntchito yonse imayenda mwapendapenda mpaka zipatso zake zimakhala zokhumudwitsa. Ino ndi nyengo ya dzinja…
Read More » -
NG’AMBA IOPSEZANSO CHAKA CHINO—UNDUNA
Chaka chatha kudali kakasi pankhani ya ulimi mvula itadula pomwe mbewu zambiri, maka chimanga, zimamasula ndipo izi zidachititsa kuti…
Read More » -
Tetezani kukokoloka kwa nthaka ndi biyo
Njira zotetezera nthaka kumadzi othamanga zili mbwee, koma katswiri wa zanthaka kusukulu yaukachenjede ya Chancellor College, Dr Jimmy Namangale,…
Read More » -
Maphunziro a chidyerano cha chimbudzi athandiza
Moyo wasintha ndipo kamphepo kayaziyazi kakudutsa tsopano m’midzi 13 yozungulira dera la T/A Njewa ku Lilongwe anthu atasintha khalidwe lochitira…
Read More » -
Lamulo lochotsa mimba ladengula
… Akufuna ogwiriridwa, opatsana pathupi pachibale ndi ana achichepere aziloledwa kuchotsa pathupi Lamulo lokhudza kuvomereza kuti amayi akhoza kumachotsa…
Read More »