Chichewa
-
Kalembera wa chisankho ayamba lolemba lomweli
Kalembera wa chisankho cha 2025 ayamba Lolemba likudzali pomwe zipani zakangalika kumema anthu ozitsatira kuti akalembetse mwa unyinji kuti adzakhale…
Read More » -
Kamangila wakwekwesa jaji
Woweruza milandu ku khoti la za chuma a Kenan Manda ati mmodzi mwa maloya odziwika a Alexious Kamangila awapepese kaamba…
Read More » -
A ‘blesser’ andipatsa mimba
Anatchereza, Ndili ndi zaka 22 ndipo ndili ku sukulu ya ukachenjedwe chaka chachiwiri. Ine ndi wochokera banja losauka kwambiri. Makolo…
Read More » -
Amanga mbusa wogwirira mwana
Apolisi m’boma la Chiradzulu Lachinayi adamanga mbusa wina wa zaka 35 pomuganizira kuti anagwirira mwana wa zaka 16 yemwe ndi…
Read More » -
Mayi adzipha ku Mulanje
Mayi wina wa zaka 29 wadzikhweza ndi nsalu ku denga la nyumba yake pa zifukwa zomwe sizikudziwika ku Mulanje. Wachiwiri…
Read More » -
MEC yakhazikika pa cha unzika pa kalembera
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latemetsa nkhwangwa pa mwala kuti ligwiritsabe ntchito chiphaso cha unzika ngati chizindikiro…
Read More » -
Mabungwe akufuna lamulo loletsa ziponda ku ndale
Mabungwe okhudzidwa ndi kayendetsedwe ka zisankho ati lamulo loletsa kugawa zinthu kwa anthu ngati njira yowakopera pa ndale (ena amati…
Read More » -
A Muluzi atseka makomo a mtopola pa ndale
Kadaulo pa ndale a Ernest Thindwa ati atsogoleri a ndale aphunzirepo pa maganizidwe a mtsogoleri wakale a Bakili Muluzi podzudzula…
Read More » -
Adandaula kusowa kwa chipatala
Amayi ochokera m’madera a mafumu aakulu Kaphuka ndi Kamenyagwaza m’boma la Dedza apempha adindo kuti ayesetse kumaliza zipatala zomwe zikumangidwa…
Read More » -
Adzudzula woswa mkazi ndi njerwa
yomwe ili m’dziko muno yomwe mtsogoleri wa dziko a Lazarus Chakwera adalengeza kuti yakhudza kwambiri maboma 23 mwa maboma 28…
Read More »