Chichewa

  • Asafuna kusaina pangano osamuvotera

    Kampeni ya zisankho za mtsogoleri wa dziko lino, aphungu a Nyumba ya Malamulo ndi makhansala yafika pa mwana wakana phala.…

    Read More »
  • CDF idatsamwitsa aphungu, makhansala

    Pomwe aphungu ndi makhansala amene agwira ntchito yawo kwa zaka 6 akwangula ntchito yawo Lachitatu, akadaulo ndi nzika zina anenetsa…

    Read More »
  • Miyezi 30 kwa ogona ndi ng’ombe

    Bwalo la Chitipa Senior Resident Magistrate, Lolemba pa 14 July 2025, lidagamula bambo wina wa zaka 24 a James Mtambo,…

    Read More »
  • Adandaula za nyumba ya chisoni

    Anthu okhala m’dera la Lisungwi m’boma la Neno adandaula ndi kusagwira ntchito kwa nyumba ya chisoni. Nyumba ya chisoni ya…

    Read More »
  • Amanga womuganizira kuba chimanga

    Bwalo la First Grade Magistrate ku Thyolo masiku apitawa lidagamula bambo Mphatso Mateyu, omwe amachokera m’mudzi mwa Changata, m’dera la…

    Read More »
  • Kampeni iyamba lolemba

    Chisankho cha 2025 chifika gawo lina Lolemba likudzali pomwe bungwe loyendetsa zisankho la MEC lidzakhazikitse misonkhano yokopa anthu. Malingana ndi…

    Read More »
  • Akufuna boma lichitepo kanthu pa za zigandanga

    Akadaulo oimira magulu osiyanasiyana ati boma likuyenera kuchitapo kanthu pa za zigandanga za zikwanje zomwe zakhala zikusokoneza zionetsero osati kungolankhulapo…

    Read More »
  • ‘Si ife oyendayenda’

    Amayi amene ali ndi mwana kapena ana koma si ali pa banja si mahule, momwe ena amaganizira, watero mlembi komanso…

    Read More »
  • Apempha kafukufuku pa CDF

    Pomwe chiwerengero cha anthu maka abambo odzipha chikupitirira kukwera m’dziko nacho chiwerengero cha achinyamata makamaka omwe ali sukulu za ukachenjede…

    Read More »
  • 6 July ili ku BNS

    Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu apempha Amalawi amene akudzapita ku chisangalalo choti dziko lino lakwanitsa zaka 61 lili…

    Read More »
Back to top button