Chichewa
-
Akhapana kaamba ka ufumu ku ntchisi
Anthu atatu akhapidwa mpaka kugonekedwa m’chipatala pa mkangano wa ufumu wa nyakwawa Kandanda kwa Senior Chief Kalumo m’boma la Ntchisi.…
Read More » -
Ena apeza golide pa vuto la mafuta
Pomwe Amalawi akulira ndi vuto la kusowa kwa mafuta a galimoto lomwe laimitsa ntchito zambiri makamaka zodalira mafutawo, anthu ena…
Read More » -
Chiyembekezo cha amalawi ku nyumba ya malamulo
Pomwe aphungu a ku Nyumba ya Malamulo akuyamba mkumano wawo wounika bajeti ya 2022-2023 pa 14 November 2022, Amalawi ati…
Read More » -
Kauniuni wa AIP watentha
Makomiti a Nyumba ya Malamulo omwe akuunika momwe feteleza wa AIP adagulidwira kuti ndalama zina zokwana K750 miliyoni zisokonekere aluma…
Read More » -
A chakwera sakugawa maswiti
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achenjeza nduna zawo kuti yense osatha ntchito yake achotsedwa paudindo wake chifukwa nduna…
Read More » -
Mwana apha bambo ake
Apolisi m’boma la Lilongwe, akusaka mnyamata wa zaka 17 pomuganizira kuti anamenya ndi kupha bambo ake a zaka 33 chifukwa…
Read More » -
Phindu lochuluka mu feteleza wa mkodzo
Ndi K12 000 yokha amagula feteleza wa mkodzo wokwana malita 20 ndi kusungunula n’kuthira m’munda. Akatero mlimiyo a Winston Devie…
Read More » -
Zaka 10 kwa bambo wofuna kugwiririra
Bwalo la milandu la majisitileti ku Kasungu Lachitatu lidagamula bambo wa zaka 26, a Geoffrey Kwenda kuti akaseweze kundende zaka…
Read More » -
Tipinduranji ku UNGA?
Mitima ya Amalawi ili dyokodyoko kudikira zomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera abweretse pochoka kumsonkhano wa atsogoleri a…
Read More » -
Achenjeza boma zoimitsa Admarc
Bungwe la ogula katundu la Consumers Association of Malawi (Cama) lati boma lalakwitsa kuimitsa ntchito za kampani yake ya Admarc…
Read More »