Chichewa
-
Apezeka ndi foni m’mimba
Nthambi ya zandende m’dziko muno yaimika kaye pantchito woyang’anira ndende Emmanuel Chiganda, yemwe mkaidi amene adapezeka ndi foni ziwiri m’mimba…
Read More » -
‘Kamuzu adali chitsime chakuya’
Pomwe Amalawi lero pa 14 May akukumbukira moyo ndi utsogoleri wa mtsogoleri woyamba a Hastings Kamuzu Banda, mizwanya pa mbiri…
Read More » -
Amalawi akupereka maganizo pa zonyonga
Komiti yoona zamalamulo m’Nyumba ya Malamulo ili mkati motolera maganizo aanthu pa zachilango chonyonga opezeka wolakwa pa milandu ya kupha,…
Read More » -
‘Sosolani mphamvu bwana’
Akadaulo a zandale ati mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akuchedwa kuthothola mphamvu zina monga momwe adalonjezera. Bungwe la…
Read More » -
Admarc yakonzeka kugula mbewu
Kampani ya boma yogula ndi kugulitsa mbewu ya Admarc yati iyamba kugula chimanga mwezi wa mawa wa May ndipo yati…
Read More » -
Aphungu akwangula zokambirana zawo
Mtsogoleri wa Nyumba ya Malamulo a Richard Chimwendo Banda adatseka mkumano wa aphungu Lachitatu ndi langizo kwa otsutsa boma kuti…
Read More » -
Mafuta atsika Lachisanu
Pamene mafuta ophikira akuyembekezeka kutsika mtengo kuyambira Lachisanu pa 1 April, komishoni yoona kuti pazikhala mpikisano wachilungamo pa malonda la…
Read More » -
Abusa awaganizira kupereka pathupi
Ali ndi zaka 17, mwanayu ankadwala matenda a muubongo omwe adabweretsanso mavuto olankhula pamoyo wake. Koma chimodzi chomwe mwanayu amakonda…
Read More » -
Boma lipereka katemera winanso wa polio
Womenyera ufulu pa nkhani zaumoyo, a George Jobe akumema makolo ndi onse omwe akusunga ana kuti aonetsetse kuti ana awo…
Read More » -
Mabishopu akunena zoona—akadaulo
Akatswiri pa nkhani za ndale adandaula ndi kusasintha kwa zinthu m’dziko lino kwa zomwe zakhala zikuchitika kwa zaka zambiri. Mwa…
Read More »