Chichewa
-
Agulitsa mwana ndi K18 miliyoni
Nkhondo ndi anansi. Wodya naye mbale imodzi ndiye amakupereka kwa adani. Izi zapherezera kwa mwana wina wa zaka 11 yemwe…
Read More » -
K5 000 yayamba kugwira ntchito
Ndalama yatsopano ya K5 000 idayamba kugwira ntchito Lachinayi pa 24 February 2022 koma Amalawi ena akuda nayo nkhawa kuti…
Read More » -
‘Takulira limodzi, kuchokera ubwana’
Lucius Banda adaimba nyimbo yomwe imati: Takulira limodzi, kuyambira ubwana…. Kusiyana kwake n’koti anthu amaimbidwa m’nyimboyo mapeto sadakwatirane. Si zili…
Read More » -
Bajeti yafika K2.84 thriliyoni
Nduna ya zachuma a Sosten Gwengwe dzulo yalengeza bajeti ya 2022 mpaka 2023 yokwana K2.84 thriliyoni ndipo ati bajetiyo yapangidwa…
Read More » -
‘Ndinkafuna mnyamata wamtali, wakuda’
Ubwenzi wa James Mdala ndi Asiyatu James unayamba pa September 22 2020, mumzinda wa Lilongwe. Awiriwo anali atakumana miyezi iwiri…
Read More » -
Anatchereza
Akuti tibwererane Anatchereza, Mmbuyomu ndidakwatiwa, koma banja lidatha ndipo ndidapeza mwamuna wina. Banja ndi mwamuna wachiwiri uja lidathanso kaamba koti…
Read More » -
Amalawi okwiya asambwadza BBC
Lachiwiri pomwe timu ya dziko lino ya Flames inkakonzekera kukumana ndi Senegal mumpikisano wa matimu a mu Africa, mtsogoleri wa…
Read More » -
2021: Chaka cha kukwera kwa katundu
Chaka cha 2021 chidali chaka cha kwera nane nkwereko wakatundu, makamaka yemwe Amalawi amadalira kwambiri pamoyo wawo wa tsiku ndi…
Read More » -
Mfumu katunga ibweretsa mpungwepungwe ku Chikwawa
Mfumu Katunga ya m’boma la Chikwawa yabweretsa mpungwepungwe polonga ufumu Gulupu Kaputeni pamene bwalo la milandu la High Court ku…
Read More » -
Covid-19 ikufala ngati moto
Komiti yoongolera zolimbana ndi mliri wa Covid-19 m’dziko muno yachenjeza kuti kachirombo koyambitsa matendawa kakufala ngati moto wolusa zomwe zachititsa…
Read More »