Chichewa
-
Zisangalalo zafika, samalani
Nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi ndi chaka chatsopano (Nyuwere) yafika koma apolisi achenjeza kuti onse osangalala mopitiriza muyeso adzakumana ndi…
Read More » -
Zokhoma mu AIP
Kugula zipangizo zaulimi zotsika mtengo kuli mkati koma pofika Lachiwiri pa 7 December 2021, alimi 1 miliyoni okha, mwa alimi…
Read More » -
Tsatsa layendaso kuchipani cha DPP
Apolisi amanga nkhwantha zitatu zachipani cha Democratic Progressive Party (DPP) powaganizira kuti anapereka malipoti abodza ku banki yokongoza maiko ndalama…
Read More » -
Mpofunika kuthana Ndi nyongolotsi
Kale alimi a m’gulu la ulimi wa ng’ombe la Chilangoma kwa T/A Kuntaja m’boma la Blantyre samapindula ndi ulimiwu kaamba…
Read More » -
Mbewu ya chimanga izigwirizana ndi dera
Ngakhale mbewu za makono zimabereka mochuluka ndipo zina zimacha msanga, akatswiri a zaulimi wa mbewu akuti mlimi amayenera asankhe mbewu…
Read More » -
Kusakasaka maphunziro
Cholinga cha mnyamatayo chidali kuyenda pansi kuchokera kwawo ku Mayani kupita ku Dedza paboma, mtunda wa makilomita 40. Iye ankalingalira…
Read More » -
Chisankho chapadera chilipolipo lachiwiri
Mabaloti achisankho chobwereza cha aphungu atatu ndi khansala mmodzi chomwe chiliko Lachiwiri likudzali afika mdziko muno dzulo (Lachisanu) ndipo bungwe…
Read More » -
Mayiyo adamukhapanso m’mutu
Bwalo la milandu ku Mangochi lagamula dotolo wina kukasewenza kundende zaka 19 atampeza ndi mlandu wogwiririra wodwala. A George Gwagwala…
Read More » -
Wokhapa mkazi wake amumanga
Zina ukamva, kamba anga mwala. Bambo wina m’boma la Ntcheu wadzipha podziponya ku galimoto yothamanga atamukhapa mkazi wake kwa Kampepuza,…
Read More » -
Theng’eneng’e pakukwera kwa mtengo wa mafuta
Theng’eneng’e labuka pakati pa boma, a mabizinesi komanso Amalawi chifukwa cha kukwera kwa mtengo wa mafuta a galimoto komanso anyale…
Read More »