Chichewa
-
DPP yakoka jekete la Tonse Alliance
Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chakokera boma la Tonse Alliance ku khothi komwe chikufuna kuti liunikile ngati kusankhidwa kwa a…
Read More » -
Chenjerani ndi mvula ya chaka chino
Nthambi yoona zanyengo yati mvula chaka chino ibwera yamphamvu moti anthu omwe amakhala m’madera momwe mumakonda kusefukira madzi achenjere ndi…
Read More » -
Anatchereza
Bwenzi langa akufuna zogonana Gogo Anatchereza, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndili pa chibwenzi ndi mnyamata wina. Koma chomwe…
Read More » -
Chitetezo cha mayeso chakhwima
Mayeso a boma a Sitandade 8, Folomu 2 ndi Folomu 4 a chaka chino aonetsa kusiyana kwa nkhwantha ndi mbatama…
Read More » -
Akwizinga Mpinganjira
Bwalo lalikulu la High Court mumzinda wa Blantyre dzulo lapeza yemwe anali mkulu wa FDH Holdings a Thomson Mpinganjira wolakwa…
Read More » -
Pali mtsutso pa zotsegulira sukulu
Pomwe unduna wa zamaphunziro watsindika kuti ophunzira a m’sukulu zogonera komweko akuunikidwa zizindikiro za Corona akafika, bungwe la aphunzitsi la…
Read More » -
‘Covid-19 akweza uchigawenga’
Apolisi ku Mzuzu ati uchigawenga wakula mwezi wa July 2021 kaamba ka mliri wa Covid-19. Nyengo ngati yomweyi chaka chatha,…
Read More » -
Mphunzitsi asamutsidwa atagona ndi mwana
Mbwanamkubwa (DC) wa boma la Nsanje a Medson Matchaya wapempha komiti ya chitukuko kwa T/A Malemia m’bomalo kuti afufuze nkhani…
Read More » -
Ukaidi kwa bambo, mayi pa zogwirira mwana
Anthuwo ndi banja. Koma lero lino laima kaye. Mwamuna akukaseweza kundende zaka 21. Mkazi wake apita kozizirako zaka 5. Masiku…
Read More » -
Opanda masiki asayende dala
Kuli cheucheu poyenda paliponse m’dziko muno kuona ngati apolisi ali pafupi makamaka kwa omwe sadachivomereze kuti masiki ikhoza kuwateteza ku…
Read More »