Chichewa
-
Mkangano wa mafumu sukuzirala
Ntchito za chitukuko zagwedera m’boma la Neno, Nsanje komanso Salima kaamba ka mpungwepungwe wa mafumu womwe sukutha. Ku Neno boma…
Read More » -
Apha mkazi ndi apongozi kaamba kothetsa banja
Mnyamata wina wa ku Mangochi wagwa m’manja mwa apolisi atapha mkazi ndi apongozi ake kaamba kothetsa banja. Stephen Sani wa…
Read More » -
Ndende zisanduka makhoti
Zanathina m’mabwalo a milandu. Sitalaka ya ogwira ntchito m’mabwalowa idasandutsa zitokosi za polisi kukhala mabwalo ozengera milandu. Izi zimachitika akuluakulu…
Read More » -
Makhoti ayambanso kugwira ntchito
Sitalaka yomwe ogwira ntchito m’makhoti amachita yatha Lachinayi. Mtsogoleri wa ogwira ntchitowa, Charles Lizigeni, adatsimikizira Tamvani kuti makhoti onse a…
Read More » -
Tidasiya kugwira vakabu—apolisi
Apolisi ati adasiya kugwira vakabu khoti litagamula kuti mchitidwewu umaphwanya ufulu wa anthu. Mneneri wa polisi James Kadadzera watsutsa zomwe…
Read More » -
Chiwerengero cha akaidi chakwera
Chiwerengero cha akaidi m’ndende za m’dziko muno chikunka chikwera. Mmodzi wa akulu owona za ndende m’dziko muno, Masauko Wiscot, wati…
Read More » -
Mavuto a ambulasi anyanya m’zipatala
Ndi Lachiwiri m’mawa. Tili pafupi ndi nyumba yachisoni pachipatala cha Gulupu mu mzinda wa Blantyre. Rose Kaphesi, mwana wake ndi…
Read More » -
Nkhondo ya mkalabongo ikadali mkati
Nthambi yoyeza katundu pamsika ya Malawi Bureau of Standards (MBS) yati nkhondo yothana ndi mkalabongo ikuyenda bwino chifukwa opanga mowawu…
Read More » -
Nkhawa akafuna kudzathandiza
Ngati satenga madzi kunyumba, amavutika akafuna kuchita chimbudzi chifukwa kumalo awo antchito kulibe madzi. Ichi ndi chibalo chomwe ogwira…
Read More » -
Anatchezera
Akunyengana ndi mnzanga Zikomo Anatchereza, Ndakhala pabanja zaka 7 ndipo tilinso ndi mwana wa zaka 7. Tsiku lina mwanayo adathyoka…
Read More »