Chichewa
-
Kwin Bee: Kulimbikitsa ufulu wa atsikana
Atsikana oimba chamba cha Afro ndi hip hop alipo ndithu m’dziko muno, koma munthu wotchula mndandandawu amayenera kusololetsa milomo yake…
Read More » -
‘Ulalo adali venda wa masiketi’
Makolo polangiza amati ukadekha, umawona maso a nkhono ndipo mwambi womwewu ansembe amati ukafuna kuvala kolona, ukuyenera kusunga khosi. Miyambiyi…
Read More » -
Ndithu chili ndi mwini
Kusankha Balaba Kumukana Yesu Usapange mistake, chonde chonde Nyimbo ya Evans Meleka idali kuphulika pa Wenela tsiku limenelo. Ya Ndirande…
Read More » -
‘Nandolo wa makono ndiye yankho’
Ngakhale mitengo ya nandolo siyinali bwino kwenikweni chaka chatha, Jonath Goliath wa m’boma la Neno akuti adachita mphumi popeza…
Read More » -
Kudya moyenera n’kofunika
Kudya ndi moyo koma woona za kadyedwe koyenera ku Lilongwe University of Agriculutre and Natural Resources (Luanar), Dr Alexander…
Read More » -
Nandolo mpatali
Ubwino wa nandolo si uli pa kupeza ndalama zochuluka kokha komanso zina zambiri, watero mkulu woona za mbewu za…
Read More » -
Aganyu okhala ndi ziphaso
Mwa zina zidabweretsa mawu woti tawuni ya Limbe imalira ochenjera, ndi kuberedwa kwa katundu ndi munthu yemwe udamukhulupirira kuti akunyamulire,…
Read More » -
Chotsani chiletso chogulitsa chimanga kunja—MCCCI
Bungwe loona za malonda ndi mafakitale la Malawi Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI) lapempha boma kuti…
Read More » -
Apempha anthu kupanga manyowa
Sukulu ya aphunzitsi Development Aid from People to People (Dapp) Chilangoma ku Blantyre yapempha anthu kupanga manyowa kuti akhale…
Read More » -
Zili bwino—PAC
Nduna yakale ya zaulimi George Chaponda yamangidwa patatha masiku 43 kuchokera pamene nthumwi kumsonkhano wa Public Affairs Committee (PAC) lidapatsa…
Read More »