Nkhani
-
Waganyu: Kulibe mipira yokonzekera zoona?
Bungwe la FAM laletsa anyamata a Flames kuti asachite zokonzekera chifukwa ndalama palibe. Pofika dzulo zidali zisadadziwike ngati Malawi isewere…
Read More » -
Amalawi 9.5 miliyoni angakhale akhungu
Bungwe logwira ntchito zopulumutsa anthu ku vuto la khungu dziko lonse la pansi la Sight Savers lati Amalawi 9.5 miliyoni…
Read More » -
Kusamvetsetsana kwabuka ku Mwanza
Kusamvetsetsana kwabuka pakati pa anthu a ku Mphete m’boma la Mwanza ndi ofesi ya DC wa bomali chifukwa cha nyumba…
Read More » -
Waganyu: Nzeru zayekha adaviyika Flames
Akulu adati nzeru zayekha adaviyika nsima m’madzi. Lero tikuti nzeru zayekha adaviyika Flames m’madzi. Zidachitika ku Algeria sindizo, timu yathu…
Read More » -
Kugawana ulamuliro kungatheke ku MW?
Pomwe mtsutso ukupitirira pa maganizo woti atsogoleri a dziko lino azigawana zigawo zozilamulira watenga malo, nduna ya zofalitsa nkhani Kondwani…
Read More » -
Okhala kumalire ku Phalombe akulira
Anthu ena ku Phalombe adandaula ndi nkhanza zimene amachitiridwa akapita m’dziko la Mozambique ndiponso ndi chiwerengero cha ana obedwa m’bomalo.…
Read More » -
Makhansala ayamba mopendama
Pamene pangodutsa miyezi 4 chisankhireni makhansala, anthu ena akudandaula kuti makhansalawa ayamba kubisala ndipo sakuwayendera kuti amve mavuto awo. Mwachitsanzo,…
Read More » -
Wa ganyu: Sesani m’nyumba
Aganyu tadza pamaso panu bwana Kondi Msungama kaamba ka mpungwepungwe omwe wamanga nthenje kutimu ya Big Bullets. Mphongo zikutsanzika kuti…
Read More » -
Dekhani pa zogawa dziko—Akadaulo
Odziwa zandale ndi malamulo ati maganizo ogawa dziko lino kuti chigawo cha kumpoto kukhale dziko loima palokha akufunika kudekha ndi…
Read More » -
‘Musachite befu ndi Ebola, takonzeka’
Amalawi asade nkhawa kuti matenda a Ebola angawakanthe chifukwa Unduna wa Zaumoyo mogwirizana ndi bungwe la zaumoyo padziko lonse la…
Read More » -
‘Mavuto a kusowa zipatala anyanya’
Ngakhale boma likuyesetsa kuti pofika 2016 likhale litamanga zipatala kuti anthu asamayende mtunda woposa makilomita 8 popita kuchitapala, Tamvani yapeza…
Read More » -
Shasha si wamankhwala
Zonga sewero zidachitika pa Kamuzu Stadium pamene Nyerere zidakokera kuuna Shasha pomukayikira kuti ndi wa timu ina yemwe amafuna achite…
Read More » -
APM wakwanitsa masiku 100 lero
Akatswiri owona mmene nkhani zandale, chuma ndi zina zikuyendera m’dziko muno komanso anthu wamba ati masiku 100 amene mtsogoleri wa…
Read More » -
Anthu aphunzitsidwe zauindo wawo—Nice
Bungwe la National Initiative for Civic Education (Nice) Public Trust lati dziko lino likulephera kutukuka chifukwa choti anthu ambiri sadaphunzitsidwe…
Read More » -
Alowerera paesiteti ya Kawalazi
T/A Kabunduli wa m’boma la Nkhata Bay wadandaula ndi anthu pafupifupi 500 omwe adalowerera ndi kukhazikika paesiteti ya tiyi ya…
Read More » -
Mikangano ya makuponi yabuka
Kulozana zala komanso kuthafulirana Chichewa chamoto zakula m’midzi polembana maina a amene adzalandire zipangizo za ulimi zotsika mtengo. Izi zikuchitika…
Read More » -
Mabungwe alimbana ndi imfa za amayi
Ngati njira imodzi yofuna kuthana ndi imfa zomwe zimadza panthawi yomwe amayi akubereka, mabungwe asanu omwe si aboma apanga chimvano…
Read More » -
Mafumu akuopa Ebola
Mantha a matenda a Ebola agwira anthu okhala m’malire a dziko lino, pamene anthu othawa m’maiko awo akulowabe m’dziko muno…
Read More » -
Chisankho cha Mulhako chilephereka
Kudali kuthafulirana Chilomwe kusukulu ya pulaimale ya Nyambadwe pulaimale Lolemba masiku apitawa pamene gulu la Mulhako wa Alhomwe ku Ndirande…
Read More » -
Waganyu: Tisaloze chala Mtawali
Sabata yatha zidatigwera, Junior Flames kupunthidwa ndi Zambia 2-1. Tisabise, Zambia idasewera bwino. Mwayi ndi goloboyi wathu, apo biii! tidakasamba…
Read More »