Nkhani
-
Kusowa kwa magazi, mankhwala ku Qech
Mavuto akhodzokera pachipatala cha Queen Elizabeth Central Hospital (QECH) mumzinda wa Blantyre. Kusowa kwa magazi ndi zipangizo kukuika miyoyo ya…
Read More » -
Chiyembekezo pa ntchito zakunja
Pamene boma lalengeza kuti likulingalira zoyambanso kutumiza achinyamata kukagwira ntchito kumaiko ena, osowa ntchito ena ati ngakhale ndondomekoyi ndi yabwino,…
Read More » -
Mavenda achita zipolowe ku Lilongwe
Zinthu zidafika povuta pamchombo wa dziko lino Lachitatu ochita malonda mumsika waukulu wa mu mzinda wa Lilongwe ataletsa munthu aliyense…
Read More » -
Chitetezo chalowa nthenya m’malawi
Chitetezo m’dziko muno chaphwasuka. Anthu akuyenda mwamantha pamene ena akuphedwa komanso katundu akubedwa molapitsa. Sabata yangothayi, zigawenga 8 zakhapa mfumu…
Read More » -
Mafumu a ku Zambia akulowerera kwa Mkanda
Pamene nkhani ya mpungwepungwe wa nyanja ya Malawi pakati pa dziko lino ndi la Tanzania ili mkamwamkamwa, nawo mafumu ena…
Read More » -
Mafumu okwezedwa ndi JB ali padzuwa
Zasolobana kumpando wa chifumu pamene mafumu ena atsopano amene adakwezedwa ndi mtsogoleri wakale Joyce Banda ayamba kuona mbonawona. Tikunenamu, mafumu…
Read More » -
Mizinda tsopano ili ndi mafumu
Patadutsa zaka 10 dziko lino lisadakhale ndi mafumu a mizinda, iyi tsopano ndi mbiri pamene mafumuwa abwereranso m’mizinda itatu ya…
Read More » -
Zaka 50 zaufulu
Ngakhale mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika akuti dziko la Malawi likuyenera kusangalala pa zomwe lakwanitsa m’zaka 50 za ufulu…
Read More » -
Alangiza boma pa kayendetsedwe ka chuma
Zipani zotsutsa boma ndi akatswiri pa kayendetsedwe kabwino ka boma ati boma lisamale kwambiri mmene liyendetsere ndalama zapadera zomwe aphungu…
Read More » -
Chisiki: Mchezo wa amayi
Pamoyo wathu pali njira zambiri zomwe timalumikizirana pophunzitsana, kugawana nzeru ndi kuunikirana. Umu ndimo moyo ulili. Ngakhale izi zili choncho,…
Read More » -
‘Chekucheku kuno ayi’
Chigamulo pamwamba pa chigamulo. Patangotha sabata imodzi bwalo lalikulu lamilandu mumzinda wa Blantyre litabwezeretsa T/A Chekucheku wa m’boma la Neno…
Read More » -
‘Mayi Mutharika ndi mlatho wa amayi’
Anthu osiyanayana ayamikira mtsogolerio wa dziko lino Peter Mutharika poganiza zokwatira atangopambana pachisankho cha pa 20 May ati chifukwa mayi…
Read More » -
MCP yakhumudwa ndi kasankhidwe ka nduna
Chipani chachikulu chotsutsa boma cha Malawi Congress (MCP) chaonetsa kusakondwa ndi mmene boma lasankhira nduna zake patatha sabata zinayi chisinthireni…
Read More » -
Mutharika asankha nduna
Pangotha maola sipikala wa Nyumba ya Malamulo Richard Msowoya atagwirizana ndi atsogoleri a zipani za m’Nyumba ya Malamulo kuti asankhe…
Read More » -
Mtima pansi—APM
Ngati aMalawi adali ndi chiyembekezo choti aona kusintha kwakukulu pachuma ndi zina ndi zina zokhudza moyo wawo pambuyo pa kulumbiritsidwa…
Read More » -
DPP yaima njiii! pa gawo 64, 65
Chipani cholamula cha DPP chagwirizana ndi zipani zotsutsa boma za MCP ndi PP kuti nkoyenera kutsata Gawo 65 la malamulo…
Read More » -
‘Ngakhale panali zovuta, chisankho chayenda’
Bungwe lophunzitsa Amalawi zosiyanasiyana kuphatikizapo za demokalase la National Initiative for Civic Education (Nice) lati ngakhale chisankho cha chaka chino…
Read More » -
Mamulumuzana agwa
Chisankho chapatatu chadza ndi zowawa zake. Pamene mpando wa pulezidenti wakhala wokokerana, mipando ya aphungu nayo yagwetsa mamulumuzana. Omwe ndi…
Read More » -
Mfundo mbweee kumtsutso
Makandideti 11 amene adasonkhana ku mtsutso wa atsogoleri usiku wa Lachiwiri m’sabatayi alonjeza zodzasintha moyo wa anthu akumudzi ngakhale makandidetiwa…
Read More » -
Akufuna T/A Chekucheku achoke
Anthu okwiya Lolemba ndi Lachiwiri m’sabatayi adasonkhana paofesi ya DC wa boma la Neno komwe amapempha bwanamkubwayo kuti achotse T/A…
Read More »