Chichewa
-
Akufuna chakudya ku Nsanje
Ngakhale maboma ambiri zikuoneka kuti apata chakudya m’nyengo ya ulimi yangothayi, anthu ena m’boma la Nsanje ati akufuna thandizo la…
Read More » -
Alandira K14 biliyoni yotukulira maphunziro
Maiko ndi mabungwe omwe amathandiza boma ati apereka thandizo la K14 biliyoni ku unduna wa zamaphunziro zotukulira maphunziro m’sukulu za…
Read More » -
Kwezani ndalama ku umoyo—MHEN
Mavuto a zaumoyo m’Malawi muno ndiye ndi osayamba. Odwala kuthinana m’zipatala, mankhwala kusowa, madotolo ochepa komanso zipatala zotalikana. Mkulu wa…
Read More » -
Chisankho chachibwereza chilipo pa 6 June
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lakhazikitsa pa 6 June 2017 kuti Amalawi adzaponye voti yachibwereza kummwera cha…
Read More » -
‘Admarc isagulitse chimanga kunja’
Bungwe la Admarc lisatengeke ndi zakuti dziko lino likhoza kukolola chimanga chochuluka chaka chino n’kugulitsa chimanga kunja padakalipano, mkulu wa…
Read More » -
Zipani zikufuna machawi pa chisankho
Zipani zandale zati bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lichititse msanga chisankho chobwereza kudera la kummwera cha ku…
Read More » -
‘Mafumu sanunkha kanthu pandale’
Kafukufuku amene achita akadaulo a zandale m’dziko muno wasonyeza kuti ngakhale mafumu ena amayesetsa kusanthula momwe Amalawi akuganizira pandale, Amalawi…
Read More » -
Lamulo latsopano la zipani alikambirana
Dziko lino lili ndi zipani zoposa 40. Komatu mwa zipanizi zisanu zokha ndi zomwe zimakangalika pomwe zina zili ziii ngati…
Read More » -
‘Chaponda abapondaponda’
Mpungwepungwe omwe udayamba n’kukayikirana pa kagulidwe ka chimanga ku Zambia, wafika pamponda chimera ndi kuchotsedwa kwa George Chaponda ngati nduna…
Read More » -
ACB idayamba kale kufufuza Chaponda
Nthambi yofufuza za ziphuphu ya Anti-corruption Bureau (ACB) yati idayamba kale kufufuza nkhani ya momwe bungwe la Admarc lidagulira chimanga…
Read More » -
Chipatala cha boma chitsekedwa loweruka
Miyoyo ya anthu pafupifupi 50 000 ozungulira chipatala cha Mkanda Health Centre m’boma la Mchinji imaikidwa pachiopsezo Loweruka chifukwa sichitsekulidwa…
Read More » -
Mtembo usagone pano—Achipatala
Pasathe tsiku mtengo wanu musadadzatenge. Uthenga omwe a zipatala za Rumphi ndi Machinga akuuza anthu chifukwa cha kuonongeka kwa malo…
Read More » -
Apolisi akuthetsa milandu ku Nthalire
Apolisi ena ku Nthalire m’boma la Chitipa akuweruza ndi kuthetsa milandu osaipititsa kubwalo la milandu. Izi zidadziwika sabata yapitayi pomwe…
Read More » -
Koma pa Wenela zidzatheka?
Tsikulo tidakhala pa Wenela. Tidali kusowa cholankhula. Kodi ndi January ameneyu? Ayi ndithu. Kukazinga chimanga chisanachoke m’munda. Nyimbo zomwe ankaika…
Read More » -
Anatchezera
Ndikufuna sukulu Zikomo Anatchereza, Ndine msungwana wa zaka 19. Sindidakwatiwepo, ngakhale sukulu ndidaisiyira Fomu 1 zaka zutatu zapitazo. Sukuluyo ndidasiya…
Read More » -
Likodzo limatha magazi m’thupi
Likodzo ndi matenda amodzi amene akapanda kuzindikiridwa msanga akhoza kupha munthu chifukwa amayamwa magazi. Michael Luhanga amene ndi katswiri pa…
Read More » -
‘Mpendadzuwa sulira madzi ambiri’
Mpendadzuwa ndi imodzi mwa mbewu zimene alimi angapindule nazo. HOLYCE KHOLOWA adacheza ndi Maxwell Chimombo wa m’mudzi mwa Cedrick kwa…
Read More » -
Mpendadzuwa ungatukule malawi
Mkulu wa bungwe la Farmers Union of Malawi (FUM) Alfred Kapichira Banda, wati pakuyenera kukhala ndondomeko yabwino pakati pa…
Read More » -
Anatchezera
Za chikondi ndi chibwenzi Agogo, Kodi chibwenzi ndi chikondi ndi zosiyana bwanji? Mwina funso limeneli likhoza kuoneka ngati lopanda nzeru…
Read More » -
Atsekera wogwiririra Gogo wa zaka 80
Bambo wa zaka 54 yemwe adagwirira gogo wa zaka 80 ku Dowa amulamula kuti akaseweze zaka ziwiri ndi theka…
Read More »