Egypt donates to Health Ministry

Health service delivery in the country is expected to improve following a donation of medical equipment from Egypt, Principal Secretary for Ministry of Health Chris Kang’ombe has said. Kang’ombe said this in Lilongwe when he officially received the donation from the Egyptian Ambassador. “The donation is a boost to Malawi’s health system because our hospitals…

Zipani zigonjera chiletso cha Escom

Zipani za ndale m’dziko muno zagwirizana ndi chiletso cha bungwe loyendetsa ntchito za magetsi m’dziko muno la Escom choti zipani zandale zisamapachike mbendera zawo pazipangizo zake monga mapolo a magetsi. Mneneri wa chipani cha MCP Jessie Kabwila wati bungwe la Escom ndi lolandiridwa paganizo lakeli, koma wapempha kuti bungweli litsate njira zabwino pochotsa mbenderazo kuopa…

Kukokana pa za amayi ovina

Zusamvana komwe kudabuka pa zakayendetsedwe ka bungwe la Asilamu la Muslim Association of Malawi (MAM) kwayamba kufalikira m’maboma ambiri tsopano. Magulu a anthu osiyanasiyana omwe akumadzitcha kuti ndi ‘Asilamu okhudzidwa’ ayamba kulankhulapo pankhani yofuna kuchotsa wapampando wa bungweli, Idrisa Muhammad, yemwe akuti akuphwanya ngodya za chiphunzitso cha chipembedzochi. Koma Muhammad watsutsa za nkhaniyi ndipo wati…

Government bemoans slow development in health sector

Minister of Finance Maxwell Mkwezalamba has said there is slow development in the health sector despite economic growth most African countries are experiencing. Mkwezalamba said this in Lilongwe on Wednesday during the opening of a three-day meeting of government and private sector officials from African countries organised by the African Development Bank (AfDB). The meeting…

Aphunzitsi akumidzi ayembekezere zokoma boma litakwenza ndalama yomwe limawapatsa powalimbikitsa kugwira ntchito kumidzi kuchoka pa K5 000 kufika pa K10 000 pamwezi. Mkulu wa bungwe la aphunzitsi la Teachers Union of Malawi (TUM), Chauluka Muwake, watsimikiza kuti ndalama yachilimbikitsoyi idakwera kuyambira mwezi wa January chaka chino ndipo aphunzitsi oyenera adayamba kale kulandira. Muwake wati kukwera…

Mabungwe omwe si aboma ati zotsatira za kafukufuku wa kubedwa kwa ndalama za boma (cashgate) kulikulu la dziko lino zomwe boma latulutsa sabata ino zangokanda pamwamba pa nkhani zikuluzikulu zomwe Amalawi amayembekezera. Mabungwewa ati imodzi mwa nkhani zikuluzikulu zomwe zotsatira za kafukufukuyu sizidachite bwino ndi kubisa maina a anthu komanso makampani omwe akukhudzidwa ndi nkhaniyi.…

Malawian youth have hope in AU, NBCC-I deal

Minister of Education, Science and Technology Luscious Kanyumba has said the memorandum of understanding (MoU) between the African Union (AU) and the National Board for Certified Councillors– International (NBCC-I) will help spur youth development in the country. Kanyumba was speaking during the signing ceremony of the MoU at the AU- Southern Africa Regional Office (AU-Saro)…

Norway committed to making Malawi green

Norwegian Ambassador Asbjorn Eidhammer says his government values the replacement of natural vegetation, especially trees which have been cut down over the decades. Eidhammer said this on Monday at Kawere Primary School in Mponela, Dowa, when he opened a tree-planting season for National Smallholder Farmers Association of Malawi (Nasfam) . “Nasfam shares the same interests with us…

Kusakaza kudaimitsa zinthu

Bungwe loyang’anira zaufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lati kusokonekera kwa kayendetsedwe ka chuma cha boma kudapangitsa kuti chitetezo chilowe pansi m’dziko muno. Mkulu wa bungweli, Sophie Kalinde, wati kusokonekeraku kudadzetsa umphawi kwa anthu ambiri zomwe zidapangitsa kuti mchitidwe wa umbava ndi umbanda ukule ndipo apolisi ntchito iwachulukire. Iye wati chifukwa chotaya…

‘Cashgate’ isokoneza khisimisi kwa a m’boma

Anthu ambiri ogwira ntchito m’boma ali pachiwopsezo chakuti Khisimisi ya chaka chino saiwona bwino chifukwa chosowa ndalama anthu ena ogwira ntchito m’boma ataba ndalama zankhaninkhani. Mpaka pano nthambi zina za boma, monga kuunduna wa zamaphunziro, sadalandirebe ndalama za November ndipo pali chikayiko kuti pofika tsiku la Khisimisi m’masiku anayi akudzawa akhala atalandira ndalama zawo. Bungwe…

Kusolola m’boma kudayamba kale

Zayamba kuululika. Kafukukufuku yemwe adapangidwa pakati pa 2009 ndi 2012 waulula kuti boma lotsogozedwa ndi chipani cha DPP, chomwe mtsogoleri wake adali Bingu wa Mutharika, lidasowetsa ndalama zoposa K90 biliyoni m’njira zopanda dongosolo. Kafukufuku wowunika njira yoyendetsera chuma cha boma ya Integrated Financial Management and Information System (Ifmis) yemwe ofesi yolondoloza chuma cha boma ya…

A ku Mozambique akulembetsa  mavoti

Nzika zina za m’dziko la Mozambique  zikulembetsa nawo m’kaundula wa mavoti ku Dedza popofuna kuti zidzavote nawo pa  chisankho cha magawo atatu chomwe chilipo pa 20 May, 2014. Mneneri wa polisi ku Dedza Edward  Kabango wati panopa apolisi anjatapo kale nzika imodzi ya dzikokolo, Edward  Tenganibwino, wa zaka 28, wochokera m’mudzi mwa Golong’ozo yemwe amafuna …

Papsa tonola, kusolola kwaphweka ku Kapitolo

Kwagwa papsa tonola kulikulu la dziko lino (Capital Hill) ku Lilongwe komwe akuluakulu ena ogwira ntchito zowerengera chuma cha boma akuyendera zija amati mbuzi imadya pomwe aimangirira. Sabata yokha ino akuluakulu awiri ogwira ntchito yowerengera ndalama za boma anjatidwa atapezeka ndi ndalama zokwana K10.8 million ndi ndalama zina zakunja zokwana $25,400 (pafupifupi K10 miliyoni) zomwe…

EU tells police to resist corruption

The European Union (EU) has urged the Malawi Police Service (MPS) to avoid indulging in corrupt practices to retain public trust on matters of security and order. EU head of delegation to Malawi, Alexander Baum made the appeal yesterday during the launch of the Malawi Police Anti-Corruption Policy in Lilongwe. He said poor incentives such…

‘Samalani ndi mitengo ina’

Kadaulo achenjeza zobzala bluegum, malaina m’munda Katswiri wa zakasamalidwe ka nthaka m’boma la Lilongwe, Edson Chagunda, wati alimi akuyenera kusankha mitengo yobzala m’munda pofuna kuthana ndi mavuto a kuonongeka kwa nthaka. Polankhula mwapadera ndi Uchikumbe, Chagunda adati pali mitengo ina yomwe imaononga nthaka komanso kumwa madzi omwe mbewu zikadagwiritsa ntchito ndi kukula bwino. Iye wati…

Clinton tips Malawi on development

Former US president Bill Clinton has urged Malawians to work hard to improve the country’s capacity on self -reliance. Clinton spoke after touring Kamuzu Central Hospital (KCH) where his Clinton Development Foundation (CHF) supports the laboratory unit with equipment and medical resources. “I have always known Malawians as hard-working people. However, I would like to…

Kaundula wa mavoti akuyenda bwino

A Malawi m’madera ena adakhamukira kumalo olembetsa maina awo m’kaundula wa chisankho cha pa 20 May 2014. Malinga ndi mphunzitsi wa za ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, izi ndi chisonyezo chakuti anthu ali ndi njala yofuna kusankha atsogoleri awo, zimene zingachititse boma la PP kugwa, kapena kulamuliranso zaka zina zisanu. Chinsinga amalankhula izi…

Mayeso alembedwanso?

Unduna wa Maphunziro wati ukudikira chikalata chochokera kubungwe loona za mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) usadalengeze ngati mayeso a Malawi School Certificate of Education (MSCE) angapitirire kapena ayi. Mneneri wa undunawu Rebecca Phwitiko adanena izi kutsatira zomwe ena amapempha undunawo kuti uimitse mayesowo chifukwa adabooka ndipo ophunzira ena adagwidwa ndi malikasa mayeso  asadalowe…