Nkhani
-
Kauniuni wa AIP watentha
Makomiti a Nyumba ya Malamulo omwe akuunika momwe feteleza wa AIP adagulidwira kuti ndalama zina zokwana K750 miliyoni zisokonekere aluma…
Read More » -
A chakwera sakugawa maswiti
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achenjeza nduna zawo kuti yense osatha ntchito yake achotsedwa paudindo wake chifukwa nduna…
Read More » -
Mwana apha bambo ake
Apolisi m’boma la Lilongwe, akusaka mnyamata wa zaka 17 pomuganizira kuti anamenya ndi kupha bambo ake a zaka 33 chifukwa…
Read More » -
Zaka 10 kwa bambo wofuna kugwiririra
Bwalo la milandu la majisitileti ku Kasungu Lachitatu lidagamula bambo wa zaka 26, a Geoffrey Kwenda kuti akaseweze kundende zaka…
Read More » -
Tipinduranji ku UNGA?
Mitima ya Amalawi ili dyokodyoko kudikira zomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera abweretse pochoka kumsonkhano wa atsogoleri a…
Read More » -
Achenjeza boma zoimitsa Admarc
Bungwe la ogula katundu la Consumers Association of Malawi (Cama) lati boma lalakwitsa kuimitsa ntchito za kampani yake ya Admarc…
Read More » -
Zipani zina sizikukhutira ndi madera a aphungu atsopano
Zipani zina za ndale m’dziko muno zati sizikukhutira ndi momwe malire atsopano a madera a aphungu ponena kuti maganizo awo…
Read More » -
Patrick Mwaungulu ndi katakwe pokankha chikopa
Patrick Mwaungulu ndi mnyamata wachichepere koma wa luso lalikulu pokankha chikopa ku timu ya Nyasa Big Bullets. Mwaungulu anasankhidwa ngati…
Read More » -
A Chilima abwera poyera
Mtsogoleri wa chipani cha UTM a Saulos Chilima womwenso ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino dzulo aulula zomwe adagwirizana…
Read More » -
Achilima awachepetsera mphamvu zaulamuliro
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati kuyambira Lachiwiri lapitali adasiya kupereka ntchito kwa wachiwiri wawo a Saulos Chilima…
Read More »