Nkhani
-
Agona ku maofesi a khonsolo ya Mzuzu
Mayi wina yemwe ndi mlembi kunthambi yoyang’anira za umoyo pakhonsolo ya mzinda wa Mzuzu, anadabwitsa anthu masiku apitawa pomwe anasamukira…
Read More » -
Woimba abedwa mumzinda wa mzuzu
Anthu a m’dera la Mchenga-utuba mumzinda wa Mzuzu akukhala mwa mantha woimba wina wodziwika m’deralo atabedwa sabata yatha. Woimbayu Dickson…
Read More » -
K34.8 biliyoni ya ngozi zadzidzidzi
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yatolera K34.8 biliyoni ya ngozi zogwa mwadzidzidzi koma ndalamazo n’zochepa poyerekeza ndi…
Read More » -
Agwidwa ndi yunifomu za polisi
Abambo ena 8 adabwitsa anthu ku Chibavi, mumzinda wa Mzuzu atapezeka ndi yunifomu zapolisi. Zovalazi ndi monga zigoba zovala panthawi…
Read More » -
Dollar yasowa
Ntchito zambiri m’dziko muno zasokonekera kapena kuima kumene potsatira kusowa kwa ndalama zakunja zomwe zimagwiritsidwa ntchito poitanitsa katundu. Umboni wafika…
Read More » -
Apezeka ndi foni m’mimba
Nthambi ya zandende m’dziko muno yaimika kaye pantchito woyang’anira ndende Emmanuel Chiganda, yemwe mkaidi amene adapezeka ndi foni ziwiri m’mimba…
Read More » -
‘Kamuzu adali chitsime chakuya’
Pomwe Amalawi lero pa 14 May akukumbukira moyo ndi utsogoleri wa mtsogoleri woyamba a Hastings Kamuzu Banda, mizwanya pa mbiri…
Read More » -
Amalawi akupereka maganizo pa zonyonga
Komiti yoona zamalamulo m’Nyumba ya Malamulo ili mkati motolera maganizo aanthu pa zachilango chonyonga opezeka wolakwa pa milandu ya kupha,…
Read More » -
Admarc yakonzeka kugula mbewu
Kampani ya boma yogula ndi kugulitsa mbewu ya Admarc yati iyamba kugula chimanga mwezi wa mawa wa May ndipo yati…
Read More » -
Aphungu akwangula zokambirana zawo
Mtsogoleri wa Nyumba ya Malamulo a Richard Chimwendo Banda adatseka mkumano wa aphungu Lachitatu ndi langizo kwa otsutsa boma kuti…
Read More »