Nkhani
-
Abusa awaganizira kupereka pathupi
Ali ndi zaka 17, mwanayu ankadwala matenda a muubongo omwe adabweretsanso mavuto olankhula pamoyo wake. Koma chimodzi chomwe mwanayu amakonda…
Read More » -
Boma lipereka katemera winanso wa polio
Womenyera ufulu pa nkhani zaumoyo, a George Jobe akumema makolo ndi onse omwe akusunga ana kuti aonetsetse kuti ana awo…
Read More » -
Mabishopu akunena zoona—akadaulo
Akatswiri pa nkhani za ndale adandaula ndi kusasintha kwa zinthu m’dziko lino kwa zomwe zakhala zikuchitika kwa zaka zambiri. Mwa…
Read More » -
Agulitsa mwana ndi K18 miliyoni
Nkhondo ndi anansi. Wodya naye mbale imodzi ndiye amakupereka kwa adani. Izi zapherezera kwa mwana wina wa zaka 11 yemwe…
Read More » -
K5 000 yayamba kugwira ntchito
Ndalama yatsopano ya K5 000 idayamba kugwira ntchito Lachinayi pa 24 February 2022 koma Amalawi ena akuda nayo nkhawa kuti…
Read More » -
Bajeti yafika K2.84 thriliyoni
Nduna ya zachuma a Sosten Gwengwe dzulo yalengeza bajeti ya 2022 mpaka 2023 yokwana K2.84 thriliyoni ndipo ati bajetiyo yapangidwa…
Read More » -
Amalawi okwiya asambwadza BBC
Lachiwiri pomwe timu ya dziko lino ya Flames inkakonzekera kukumana ndi Senegal mumpikisano wa matimu a mu Africa, mtsogoleri wa…
Read More » -
2021: Chaka cha kukwera kwa katundu
Chaka cha 2021 chidali chaka cha kwera nane nkwereko wakatundu, makamaka yemwe Amalawi amadalira kwambiri pamoyo wawo wa tsiku ndi…
Read More » -
Mfumu katunga ibweretsa mpungwepungwe ku Chikwawa
Mfumu Katunga ya m’boma la Chikwawa yabweretsa mpungwepungwe polonga ufumu Gulupu Kaputeni pamene bwalo la milandu la High Court ku…
Read More » -
Covid-19 ikufala ngati moto
Komiti yoongolera zolimbana ndi mliri wa Covid-19 m’dziko muno yachenjeza kuti kachirombo koyambitsa matendawa kakufala ngati moto wolusa zomwe zachititsa…
Read More »