Nkhani
-
Ufulu usasokoneze umunthu, chipembedzo
Pomwe dziko la Malawi lakwanitsa zaka 60 mu ufulu wodzilamulira, atsogoleri ena a mipingo ati zili bwino komanso pakuyenera kusamalitsa…
Read More » -
Anjata opezeka ndi mfuti
Apolisi ku Namwera m’boma la Mangochi amanga abambo awiri omwe angotulutsidwa kumene kundende popezeka ndi mfuti ya mtundu wa Retay…
Read More » -
Amangidwa zaka 14 atagonana ndi mwana
Bwalo la milandu ku Balaka lalamula a Steven Maluwa a zaka 24 za kubadwa kuti akakhale kundende zaka 14 kaamba…
Read More » -
Mtsutso pa kupikisana nawo kwa olowa zipani
Pamene zipani zina zalengeza zochititsa misonkhano yake yaikulu, pali mtsutso pakati pa akadaulo a ndale pamene zipanizo zikunena kuti sizikufuna…
Read More » -
Zipolowe za ndale zikuyala
Magulu osiyanasiyana kuphatikizapo zipani za ndale ati apolisi asaonerere zipolowe zokhudza ndale zomwe zikuchitika m’dziko muno pounikira kuti zoterezi zimatha…
Read More » -
Kulankhula ndi Habakuku, K1 miliyoni igwe kaye
Masiku apitawa, mtsogoleri wa mpingo wa ECG-Jesus Nation a Shepherd Bushiri adapereka K6 miliyoni kwa Prophet Habakuku, yemwe amatchuka pa…
Read More » -
Alira atamasulidwa
Misonzi inagwa kuti lakataaaa! m’masaya a Dennis Dias ngati namondwe bwalo la Senior Resident Magistrate ku Mangochi litawamasula pa mlandu…
Read More » -
‘Tonse ikubisa thumba la tambe’
Abwenzi akuluakulu mumgwi r izano wa Tonse Alliance a UTM komanso People’s Party (PP) akana kulankhulapo p a z omwe…
Read More » -
Adzudzula mawu a APM
Akadaulo pa ndale komanso mabungwe omwe si a boma omwe amaunikira za kayendetsedwe ka zisankho ati mawu onyozana kapena kufalitsa…
Read More » -
Apulumuka lokumbakumba atadya chiphe kuyesa mpama
Anthu 15 a m’mudzi wa Kalonga mfumu yaikulu Mlolo koma anasamukira kwa Milton TA Mbenje m’boma la Nsanje Lamulungu abwerera…
Read More »