Nkhani
-
Apempha alembe aphunzitsi ena
Kadaulo pa za maphunziro a Benedicto Kondowe wati boma likusempha chisa popitiriza kusula aphunzitsi pomwe aphunzitsi ena oposa 9 000…
Read More » -
Magulu othandiza odwala edzi akufa
Chitsime chidauma! Moti magulu 132 mwa 150 olimbana ndi mlili wa edzi mu mzinda wa Mzuzu afa pamene ena 18…
Read More » -
Akana tsankho pa maphunziro
Ophunzira olumala apitirira kukumana ndi mavuto kaamba koti apatsidwa ndalama zochepa mu bajeti ya 2021/22 poyerekeza ndi alunga. Gulu la…
Read More » -
Wogwira ‘kumaso’ kwa mchemwali wake achimina
Bambo wina wa zaka 32 ku Salima akunong’oneza bondo pano kaamba kosaugwira mtima mpaka kufuna kugonana ndi mchemwali wake. Nkhaniyo…
Read More » -
Akapizana madzi amoto poganizirana miseche
Mayi wa zaka 21 Tionge Gerald ku Mponela m’boma la Dowa wakapiza madzi a moto mkazi mzake Lydia Tembo wa…
Read More » -
‘Boma litisamale pa nkhani ya malo’
Alimi ena ang’onoang’ono m’maboma a Mulanje komanso Thyolo achenjeza boma kuti lisanyozere madandaulo awo akusowa kwa malo ponena kuti maesiteti…
Read More » -
Anthu 49 afa ndi mphenzi
Mphezi zavuta chaka chino. Pofika lero anthu 49 aphedwa ndi mphenzi chiyambireni nyengo ya mvula, poyerekeza ndi 32 omwe adafa…
Read More » -
Luso la Joe Kellz mpatali
Kellz ndi katakwe ku nkhani ya maimbidwe. Mwachidule, tingoti Kellz amatha. Masiku apitawa iye adatulutsa nyimbo yokumbukira luso la katswiri…
Read More » -
Tambala walira
Chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chapeza mipando 4 mwa mipando 7 ya aphungu yomwe zipani komanso oima paokha amalimbirana…
Read More » -
Aphunzitsi akhoza kuyambanso sitalaka
Masiku 7 omwe bungwe la aphunzitsi la Teachers Union of Malawi (TUM) lidapereka ku boma kuti liwapatse ndalama zomwe adapangana…
Read More »