Nkhani
-
Chitetezo cha mayeso chakhwima
Mayeso a boma a Sitandade 8, Folomu 2 ndi Folomu 4 a chaka chino aonetsa kusiyana kwa nkhwantha ndi mbatama…
Read More » -
Akwizinga Mpinganjira
Bwalo lalikulu la High Court mumzinda wa Blantyre dzulo lapeza yemwe anali mkulu wa FDH Holdings a Thomson Mpinganjira wolakwa…
Read More » -
Pali mtsutso pa zotsegulira sukulu
Pomwe unduna wa zamaphunziro watsindika kuti ophunzira a m’sukulu zogonera komweko akuunikidwa zizindikiro za Corona akafika, bungwe la aphunzitsi la…
Read More » -
‘Covid-19 akweza uchigawenga’
Apolisi ku Mzuzu ati uchigawenga wakula mwezi wa July 2021 kaamba ka mliri wa Covid-19. Nyengo ngati yomweyi chaka chatha,…
Read More » -
Mphunzitsi asamutsidwa atagona ndi mwana
Mbwanamkubwa (DC) wa boma la Nsanje a Medson Matchaya wapempha komiti ya chitukuko kwa T/A Malemia m’bomalo kuti afufuze nkhani…
Read More » -
Ukaidi kwa bambo, mayi pa zogwirira mwana
Anthuwo ndi banja. Koma lero lino laima kaye. Mwamuna akukaseweza kundende zaka 21. Mkazi wake apita kozizirako zaka 5. Masiku…
Read More » -
Opanda masiki asayende dala
Kuli cheucheu poyenda paliponse m’dziko muno kuona ngati apolisi ali pafupi makamaka kwa omwe sadachivomereze kuti masiki ikhoza kuwateteza ku…
Read More » -
Ana akagonana azimangidwa?
Bwalo lalikulu la milandu Lachitatu likudzali likhala likumva mlandu umene mnyamata wina wa zaka 15 (sitimutchula dzina) wasumira boma. Mnyamatayo…
Read More » -
Esiteti, anthu ayanjana pa za malo
Esiteti ya Lujeri yalola anthu pafupifupi 5 000 amene adalowerera malo a esitetiyo ku Mulanje kuyambira zaka za m’ma 2000…
Read More » -
Apolisi azilembanso mayeso a malamulo
Patadutsa zaka 20 apolisi asakulemba mayeso okhudza zomwe malamulo a ntchito yawo amanena omwe m’Chingerezi amatchedwa Service Standing Order (SSO),…
Read More »