Nkhani
-
Ayesa zida za Ebola
Patangodutsa sabata zitatu munthu wina wa m’boma la Karonga ataganiziridwa kuti ali ndi Ebola, aboma ayamba kuyesa zida zothandiza odwala…
Read More » -
Adzudzula MEC
Katswiri wa ndale wa sukulu yaukachenjede ya University of Livingstonia (Unilia), George Phiri, wati bungwe la MEC lidalakwa kuimitsa chisankho…
Read More » -
Kutentha koonjeza kuzinga maiko
A nthambi yoona za nyengo m’dziko muno auza Amalawi kuti alimbe mtima chifukwa nyengo yotentha yomwe yakhala m’dziko muno kwa…
Read More » -
Lero moto, mawa moto!
Pali mtunda kuti dziko lino likhale lodzidalira pothana ndi ngozi zamoto pamene zadziwika kuti makhonsolo m’dziko muno alibe zipangizo zokwanira…
Read More » -
Mvula yayandikira, makuponi kulibe
Pamene ndondomeko yogawa makuponi imayembekezeka kutha dzulo, Tamvani m’sabata ikuthayi idapeza kuti madera ena ndondomeko yolemba olandira komanso kugawa makuponi…
Read More » -
Kupewa moto mu Dzalanyama kuteteza madzi
Anthu ozungulira nkhalango ya Dzalanyama m’maboma a Lilongwe ndi Mchinji awapempha kuti apewe kuyambitsa moto mwachisawawa kuti ateteze ndi kusamalira…
Read More » -
Amalawi aona sabata yakuda
Pomwe Amalawi akuyembekeza zotsatira za mlandu wa chisankho, sabata ikuthayi kwakhala kuli mpungwepungwe ku Malawi. Kwa Msundwe ku Lilongwe kudali…
Read More » -
Mwapasa autsa mapiri
Pamene pali kusamvana pakati pa aphungu a Nyumba ya Malamulo pa zovomereza Duncan Mwapasa kukhala mkulu wa apolisi m’dziko muno,…
Read More » -
Apolisi amanga mayi wa mwana womwa kachasu
Apolisi ku Chirimba mu mzinda wa Blantyre akwizinga mayi wa mwana ndi anzake awiri powaganizira kuti amalekerera ndi kuyamikira mwana…
Read More » -
Dziko layaka moto, Bushiri wachenjeza
Mneneri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) Shepherd Bushiri wachenjeza atsogoleri andale kuti mpungwepungwe womwe uli m’dziko muno utha…
Read More »