Nkhani
-
Apolisi amanga mayi wa mwana womwa kachasu
Apolisi ku Chirimba mu mzinda wa Blantyre akwizinga mayi wa mwana ndi anzake awiri powaganizira kuti amalekerera ndi kuyamikira mwana…
Read More » -
Dziko layaka moto, Bushiri wachenjeza
Mneneri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) Shepherd Bushiri wachenjeza atsogoleri andale kuti mpungwepungwe womwe uli m’dziko muno utha…
Read More » -
Malawi ikuswapangano la UN
Malawi ikuswa pangano la zaumoyo la bungwe la United Nations (UN) lomwe idasaina ku Abuja m’dziko la Nigeria. Akatswiriwa akuti…
Read More » -
Chimanga cha k1bn chaola ku admarc
Komiti ya za malimidwe ku Nyumba ya Malamulo yatulukira kuti chimanga cha ndalama zokwana K1 billion chaola mu nkhokwe za…
Read More » -
Mutharika afika mawa
Mtsogoleri wa dziko lino, Peter Mutharika, afika m’dziko muno mawa kuchokera ku America komwe adakakhala nawo pa msonkhano wa bungwe…
Read More » -
Chipwirikiti pa Malawi
Zomwe zikuchitika m’dziko la Malawi zaimitsa mitu ya anthu kuphatikizapo akadaulo pa nkhani zosiyanasiyana. M’sabata yomwe ikuthayi, zionetsero zomwe zidaima…
Read More » -
HRDC ikufunabe zionetsero m’zipata
Gulu lomwe likutsogolera zionetsero zofuna kuchotsa wapampando wa bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane Ansah la Human Rights Defenders…
Read More » -
Mwapasa achoke—HRDC
Zipani za Malawi Congress Party (MCP) ndi UTM Party zati ziunika mwakuya ganizo la mgwirizano wa mabungwe omenyera ufulu wa…
Read More » -
Zionetsero zaima
Anthu zikwizikwi adabwerera manja ali m’khosi kuchoka m’malo a zionetsero Lachitatu pa 28 August 2019 atauzidwa kuti zionetserozo zalephereka kaamba…
Read More » -
Mtunda ulipo pa zokambirana
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Bakili Muluzi sali kutali kwenikweni ndi khumbo lake lofuna kukumana ndi atsogoleri a Human Right…
Read More »