Chichewa
-
Azula mitanda kumanda
Bambo wina wa m’mudzi mwa Mikayeli, kwa Mfumu Zulu, m’boma la Mchinji walaula dziko atakazula mitanda pa mitumbira isanu chifukwa…
Read More » -
MLS yalasa!
Bungwe la akadaulo a za malamulo m’dziko muno la Malawi Law Society (MLS) ladzudzula zipani za ndale, mkulu wa bungwe…
Read More » -
Amalawi abwerera kumsewu
Amalawi ena amene akufuna kuti wapampando wa bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane Ansah atule pansi udindo,…
Read More » -
CMST iyambanso kugawa mankhwala
Nkhokwe ya mankhwala ya Central Medical Stores Trust (CMST) yatsiriza kukambirana ndi mabungwe omwe amathandiza dziko lino pa nkhani ya…
Read More » -
MEC yachotsa maina 13 244 m’kaundula
Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lachotsa m’kaundula maina 13 244 omwe eni ake adawalembetsa kopotsera kamodzi zomwe lati n’zotsutsana…
Read More » -
Anthu ambiri sakupita kukatsimikiza maina
Ntchito yotsimikiza maina m’kaundula wa zisankho za chaka cha m’mawa ili pendapenda kaamba koti anthu ambiri saonetsa chidwi chopita kukaona…
Read More » -
‘Abambo zawakanika, yesaniko amayi’
Bungwe lomwe likumenyera kuti amayi akhale m’maudindo la Ligowe Community Development Organisation (Licodo) lamemeza anthu a boma la Neno ndi…
Read More » -
‘Ife toto takana!’
Mkozemkoze adanyula maliro aeni. Sinodi ya Livingstonia yatemetsa nkhwangwa pamwala kuti sipepesa monga momwe mafumu ena m’boma la Rumphi alamulira.…
Read More » -
Kafukufuku wa chamba watha
Zotsatira za kafukufuku wa ulimi wa chamba zomwe Amalawi akhala akudikira zatuluka koma mlembi wa unduna wa zamalimidwe, mthilira ndi…
Read More » -
Chitonzo pa matenda
Kutentha kwa mwezi wa November kwamufoola. Alibe nsapato kuphazi komabe akuyesetsa kudzikoka limodzi ndi mayi ake—a zaka 71—kuti akafike kuchipatala…
Read More »