Chichewa
-
‘Kasanthuleni za chisankho’
Pamene aphungu a Nyumba ya Malamulo akukonzekera kukumana kuyambira Lolemba likudzali, akadaulo ena awapempha kuti akalunjike pa za chisankho cha…
Read More » -
Anthu 6.9 miliyoni alembetsa mavoti
Zotsatira za kalembera wa mavoti zomwe bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) latulutsa zasonyeza kuti anthu 6 856 295 ndiwo…
Read More » -
‘2019 ikudetsa nkhawa’
Chikhulupiliro chapita. Amalawi 28 mwa 100 aliwonse akuti akuona chisankho chopanda mtendere ndi chilungamo chaka cha mawa. Izi zadziwika potsatira…
Read More » -
‘Obwereza MSCE adzionere njira’
Unduna wa zamaphunziro wati siungachite kulembetsa mayeso apadera ophunzira 72 542 omwe adalakwa mayeso a Malawi School Certificate of Education…
Read More » -
Apolisi athotha gulu la MYP
Asilikali 56 a gulu la chitetezo la mtsogoleri wakale, Hastings Kamuzu Banda la Malawi Young Pioneer (MYP) ali zungulizunguli mu…
Read More » -
‘Tataya nanu chikhulupiriro’
Kwayaka moto! Zipani zina zotsutsa zati zilibenso chikhulupiriro ndi mkulu wa bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane…
Read More » -
MEC idzudzula UTM
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission(MEC) ladzudzula gulu la United Transformation Movement (UTM) pokhala nawo m’misonkhano ya bungwe loyang’anira…
Read More » -
Olembetsa akuchepa
Boma la Nsanje likupitilirabe kutsogola pa maboma omwe nantindi wa anthu alembetsa pa ntchito ya kalembera wa m’kaundula wachisankho cha…
Read More » -
Akulipitsa kulembetsa khadi
Anthu ena amene sadalembetse nambala zawo akulirira kuutsi pamene ma agenti ena akuwauza kuti alipire ngati akufuna nambala yawo ilembetsedwe.…
Read More » -
Chisankho chopanda mudyo?
Kodi azitaya? Chisankho cha 2019 ena sakuchionetsa dovu pamene zipani 12 zimene zidatulutsa atsogoleri mu 2014, zinayi zokha pakadalipano ndi…
Read More »