Chichewa
-
Chipulula mu DPP
Masankho a ndime ya chipulula (mapulaimale) ayamba ndi moto m’chipani cha Democratic Progressive Party (DPP). Lolemba lapitali yemwe adali mkulu…
Read More » -
Ayamba kugawa makuponi
Nduna ya malimidwe Joseph Mwanamvekha yapempha alimi kuti asagulitse makuponi awo amene boma lidayamba kupereka Lachinayi. Ndunayo idakhazikitsa ntchito yopereka…
Read More » -
Angwanjula osalembetsa
Ngati mukuyesera kuimba foni koma sizikutheka, kapena mayunitsi sakulowa, ingodziwani kuti nambala yanu sidalembetsedwe ndipo ayithothola. Izi ndi zomwe anthu…
Read More » -
Kulumana pa ofunika kulandira chakudya
Kusankha ovutikitsitsa kuti alandire thandizo la chakudya kuchokera ku boma kwavuta m’midzi ina pamene anthu ndi mafumu ayamba kulumana. Izitu…
Read More » -
Kusamvana pa zochotsa fizi
Ganizo la boma lochotsa fizi pa maphunziro m’sukulu za sekondale ladzetsa chisokonezo m’sukulu zaboma zina pomwe ophunzira ena akukana kulipira…
Read More » -
Akana kulemba UTM
Akatswiri pa nkhani za ndale ati mlembi wa zipani sadalakwitse pokana kulemba UTM ngati chipani m’dziko muno. Wachiwiri kwa mlembi…
Read More » -
Sensasi ili mkati
Pamene kalembera wa anthu ndi nyumba ali mkati, mafumu ena ati akuyembekezera kuti mavuto amene amakumana nawo achepa chifukwa boma…
Read More » -
‘Zipani zisaope achinyamata’
Bungwe lolimbikitsa achinyamata pa ndale mu Africa la Centre for Young Leaders in Africa (CYLA), lapempha zipani zandale m’dziko muno…
Read More » -
Sitilemba akunja—Ansah
Pamene kalembera wachisankho walowa gawo lachisanu, mkulu wa bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane Ansah wati Amalawi…
Read More » -
‘Mgwirizano ungathetse zipolowe’
Mgwirizano pakati pa atsogoleri, ngakhale asemphane maganizo pa ndale ndiko kungathetse zipolowe ndi mikangano ya ndale, atero akadaulo. Iwo adanena…
Read More »