Chichewa
-
Maliro akapeza ukwati
Pamoyo wa munthu, mavuto kapena mtendere zimabwera mosayembekezera. Nthawi zina zovuta zimagwa pamene pali zilinganizo zina zachimwemwe monga ukwati.…
Read More » -
Zipolowe ku mapulaimale
chotsutsa cha MCP chidaimitsa mapulaimale ake kaamba ka zipolowe ku Dedza, zipani zandale, kuphatikizapo MCP, zatsindika kuti zichilimika kuti zipolowe…
Read More » -
Achinyamata akambirana za m’manifesto
Nthambi ya achinyamata ya chipani cha Malawi Congress Party (MCP) yakambirana mfundo zokhudza achinyamata zomwe chipani chawo chiyike m’manifesto…
Read More » -
Alimi otsogola amasamalira nthaka
Chuma chili mu nthaka, komatu sichipezeka mu nthaka yosakazidwa. Kusasamala za chilengedwe monga mitengo kukupangitsa kuti nthaka iziguga. Izitu…
Read More » -
Kupherera ng’amba ndi Akalozera m’munda
Alangizi a zaulimi apempha alimi m’dziko muno kuti azipanga akalozera kuti ateteze nthaka, komanso kusunga chinyontho kwa nthawi yaitali…
Read More » -
TB imakhudza ziwalo zonse
Kusiyana ndi nthenda zina, nthenda ya chifuwa chachikulu ya TB imakhudza chiwalo china chilichonse, kupatula zikhadabo ndi tsitsi, watero…
Read More » -
Anthu 500 000 sadalembetse
Zotsatira za kalembera wachisankho m’gawo loyamba ndi lachiwiri zasonyeza kuti anthu 468 860 omwe amayenera kulembetsa sadalembetse nawo m’kaundulayo. Malingana…
Read More » -
Adzudzula Admarc
Mafumu ndi alimi ena m’zigawo zonse zitatu adandaula kuti msika wa Admarc watsegulidwa mochedwa iwo atagulitsa kale chimanga chawo motchipa…
Read More » -
Kalembera wafika kummwera
Kalembera wa mkaundula wachisankho cha chaka cha mawa wafika m’chigawo cha kummwera tsopano ntchitoyi itakumana ndi zokhoma zosiyanasiyana m’maboma a…
Read More » -
Kuli ziii! za mapulaimale
Pamene ntchito ya kalembera wa chisankho cha pa 21 May 2019 walowa m’gawo lachinayi, zipani zandale zikuluzikulu zikadali duuu, osafuna…
Read More »