Chichewa
-
Mamonitala ena sakupezeka kolembetsa
Mamonita a zipani zina sakupezeka m’malo olembetsera mavoti, Tamvani wafukula. Mmalo 7 a m’midzi yomwe Tamvani adazungulira mkati mwa sabatayi,…
Read More » -
‘Mafumu akusunga zitupa za ena’
Pamene gawo lachitatu la kalembera wa chisankho cha pa 21 May 2019 akuyembekezeka kutha mawa m’boma la Lilongwe, anthu ena…
Read More » -
MCP siidakhutire ndi kalembera
Chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chati ngakhale ndime yachiwiri ya kalembera wa zisankho yayenda bwino poyerekeza ndi yoyamba, MEC…
Read More » -
UDF siidaganize za mgwirizano—Atupele
Phungu wa chipani cha United Democratic Front (UDF) wakummwera kwa boma la Balaka, Lucius Banda, wapempha chipanicho kuti chilowe mu…
Read More » -
UTM Ilembetsa ngatichipani—Malunga
Ulendo wapsa. Ali ndi mwana agwiritse. Eni basiyo akuti siiphwa matayala mpaka ikafika ku zisankho zapatatu za chaka cha mawa.…
Read More » -
Chilima akhazikitsa UTM ku Blantyre
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Chilima, mawa akhazikitsa gulu la United Transformation Movement (UTM) ku Njamba mu mzinda…
Read More » -
Wodzaima pa mpando wa pulezidenti azapereka K2m
Bungwe la Malawi Electoral Support Network (Mesn) ladzudzula bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) pokweza ndalama zomwe anthu ofuna kudzaima…
Read More » -
MEC, MCP yakhutira ndi kalembera
Zinthu zasintha. Anthu akulembetsa mwaunyinji m’gawo lachiwiri la kalembera wa zisankho zomwe zidzachitike m’dziko muno chaka cha mawa. Mkulu wa…
Read More » -
La 40 lakwana kwa womata anthu phula
Wakhala akumata anthu phula m’midzi kuti amupatse ndalama ndipo adzakhala ndi mwayi wopeza ngongole kuchokera ku bungwe la Emmanuel International.…
Read More » -
‘Zovota ife ayi’
“Anthu opotsa 3 000 adalembetsa unzika m’dera langa. Lero anthu 1 240 okha ndiwo alembetsa kalembera wa zisankho.” Izi ndizo…
Read More »