Nkhani
-
Adzudzula MEC
Magulu osiyanasiyana okhudzidwa ndikayendetsedwe kazisankho adzudzula bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) posintha masiku odzachita kalembera wa kaundula…
Read More » -
Tikumafa nthawi ya chisankho achialubino adandaula
Anthu ambiri m’dziko muno akugwedezabe mitu ndi nkhani yomwe inachitika ku Kasungu. Kumeneko, apolisi anamanga mayi wina yemwe amachokera m’mudzi…
Read More » -
Woganiziridwa kuzembetsa anthu wagwidwa
Mwambi woti khoswe wa pa tsindwi adaulula wa pa dzala wapherezera ku Mulanje komwe mlandu wa pa msewu wavumbulutsa mulandu…
Read More » -
Msonkhano wa UTM walephereka
Msonkhano womwe komiti yaikulu ya chipani cha UTM imayenera kukhala nawo walephereka. M l e m b i w a…
Read More » -
Musandinjate, ndinali ku ndende komweko
A Jonathan Ng’ambi Lachinayi sabata yatha adaseketsa omvera milandu m’khoti la Chitipa atapempha woweruza milandu kuti asawapititse ku ndende ati…
Read More » -
Ozunza mwana avomera mlandu
Bwalo la milandu ku Balaka lati pa 18 July lidzapereka chilango kwa mayi Lilian Matako omwe Lachisanu adavomera mlandu woti…
Read More » -
Woima ndi pulezidenti azikhala wotani?
Mwezi wa June 2025 onse ofuna kudzapikisana nawo pa chisankho cha Pulezidenti adzakhala akupereka kalata zawo ku bungwe la Malawi…
Read More » -
Ufulu usasokoneze umunthu, chipembedzo
Pomwe dziko la Malawi lakwanitsa zaka 60 mu ufulu wodzilamulira, atsogoleri ena a mipingo ati zili bwino komanso pakuyenera kusamalitsa…
Read More » -
Anjata opezeka ndi mfuti
Apolisi ku Namwera m’boma la Mangochi amanga abambo awiri omwe angotulutsidwa kumene kundende popezeka ndi mfuti ya mtundu wa Retay…
Read More » -
Amangidwa zaka 14 atagonana ndi mwana
Bwalo la milandu ku Balaka lalamula a Steven Maluwa a zaka 24 za kubadwa kuti akakhale kundende zaka 14 kaamba…
Read More »