Chichewa
-
Aphana pachibale kaamba ka malo
Apolisi m’boma la Lilongwe amanga abambo atatu a banja limodzi powaganizira kuti adapha mbale wawo polimbirana malo m’mudzi mwa Maliseni…
Read More » -
Loans board struggles to recover K16bn
The Higher Education Student’s Loans and Grants Board (HESLGB) says it is struggling to recover K16 billion from its beneficiaries.…
Read More » -
Mlandu wa a Bushiri ukhalako pa Julayi 10
Mlandu wa a Pulofeti Shepherd Bushiri ndi akazi awo a Mary unalephereka kuyamba Lachiwiri kaamba ka kusagwirizana kumene kunalipo pakati…
Read More » -
Centre turns to parley on rising food costs
The Centre for Social Concern (CfSC) has urged members of Parliament to discuss and pass the Right to Food Bill…
Read More » -
Chomwe aimitsira mlandu wa a muluzi chidziwika lolemba
Mkulu wa bungwe loyendetsa milandu la Director of Public Prosecutions (DPP) a Masauko Chamkakala akuyembekeza kuuza Amalawi chifukwa chomwe aimitsira…
Read More » -
MEC yakonzeka kulanga osokoneza
Chisankho cha 2025 chikhoza kuzakhala umboni wa ulamuliro weniweni wa demokalase ngati bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lizatsate malamulo…
Read More » -
Umitsani chimanga mokwanira ngakhale mvula ikugwabe
Adathawitsa chimanga m’munda chisadaumitsitse kuopetsa kuti chionongeka ndi mvula imene ikupitirirabe kugwa m’dziko muno komanso akuba amene akuba mopanda chisoni.…
Read More » -
Azengedwa mlandu wopha mkazi wake ku mangalande
Nyuzipepala zikuluzikulu za ku Mangalande Lachisanu zidadzala ndi nkhani ya bambo wina wa ku Malawi amene akumuganizira kuti adabaya ndi…
Read More » -
Mpungwepungwe ku msika wa fodya
Kudali mpungwepungwe kumsika wa fodya wa Kanengo mumzinda wa Lilongwe pomwe alimi adakwiya ndi mitengo ya fodya ndipo adauza ngakhale…
Read More » -
Mneneri akhala osadya komanso kumwa masiku 40
Mneneri Ellason Zande akuti anafa n’kudzukanso pomwe anasala kudya kwa masiku 40, Mulungu atawaonekera. A Zande omwe akuchita utumiki wawo…
Read More »